Chichewa 7

  • ㆍISBN : 9788928231294
  • ㆍPages : 369

Ndemanga ndi Ziphunzitso za mu Buku la Chivumbulutso - KODI NTHAWI YA WOSUSA KHRISTU, KUPHEDWA KWA AKRISTU, KUKWATULIDWA NDI UFUMU WA ZAKA CHIKWI CHIMODZI IDZABWERA? (Ⅰ)

Paul C. Jong

Chitapita chipolowe chazigewenga cha 9/11, mafunso ku “www.raptureready.com” Intaneti saiti pankhani ya nyengo, anachulukira kufika ku mamiliyoni opitilira ku 8 anafika, malinga ndi kafuku-fuku wa CNN ndi TIME, ma Ameleka opitilira pa 59% akhulupilira mkukwatula kosilizira.
Kunena za nyengo, mlembiyu akunena mfundo zeni-zeni za mutu wa buku la Chivumbulutso, kunenanso zakubwera kwa Wosusa Khristu, kuphedwa kwa oyera ndikukwatulidwa kwao, Ufumu wa zaka Chikwi chimodzi, ndi Kumwamba kwa Tsopano ndi Dziko la tsopano-zonse kulingana ndi Malembo wonse ndiponso motsogoleledwa ndi Mzimu Woyera.
Bukuli limapatsa ndemanga za ndime ndi ndime mu Buku la Chuvumbulutso powonjezedwa ndi ziphunzitso zozama za mlembi. Aliyense amene amawerenga bukuli adzadziwa zolinga zonse zimene Mulungu anasungira dzikoli lapansi.
Tsopano ndi nthawi kuti inu mdzindikire chofunikira cheni-cheni mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, kotero kuti mupeze nzeru zimene zingakuomboleni kuchoka ku mayetsero onse ndi masautso a nthawi yamapeto. Ndi mabukuwa awiri, ndiponso pokhulupilira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, mdzakwanitsa kupambana mayetsero onse ndi masautso ananeneredwa mu Chivumbulutso.

AUDIOBOOK
undefined
Due to COVID-19 and disruption to international mail service
we have temporally suspended our ‘Free Print Book service’.
In the light of this situation we are not able to mail you the books at this time.
Pray that this pandemic will end soon and the resumption of the postal service.