Chichewa 8

  • ㆍISBN : 9788928231522
  • ㆍPages : 499

Ndemanga ndi Ziphunzitso za mu Buku la Chivumbulutso - KODI NTHAWI YA WOSUSA KHRISTU, KUPHEDWA KWA AKRISTU, KUKWATULIDWA NDI UFUMU WA ZAKA CHIKWI CHIMODZI IDZABWERA? (Ⅱ)

Paul C. Jong

Akristu Ambiri matsiku ano okhulupilira mchiphunzitso cha kukwatulidwa kosaona-chisautso. Cifukwa iwo okhulupilira mchiphunzitsocho chachinyengo chowaphunzitsa kuti iwo adzatengedwa Chisautso Chachikulu cha zaka 7 chisanabwere, okhala moyo wachipembezo osatangwanidwa okhutilisidwa.
Koma kukwatulidwa kwa oyera kudzachitika pokhapo miliri ya malipenga 7 yatsiliza nchito yake mpaka muliri wa 6 wonse utathilidwa-ndi pamene, kukwatulidwa kudzachitika Wosusa Khristu ataonekera pakati mtsokonozo wa dziko lonse lapansi ndipo oyera obadwa-mwatsopano ataphedwa, ndiponso ngati lipenga la 7 lalizidwa. Ndi pa nthawi imeneyo pamene Yesu adzatsika kuchoka Kumwamba, ndipo chiukitso ndi kukwatulidwa kwa oyera obadwa-mwatsopano chidzachitika (1 Atesalonika 4:16-17).
Pa tsikuli, wina aliyense mdzikoli lapansi adzakhala ali kuimilira pa mphatukano za miseu wa kumalo ake osatha. Olungama amene anabadwa mwatsopano pokhulupilira mu “uthenga wa madzi ndi Mzimu” adzaukitsidwa ndi kukwatulidwa, ndipo adzakhala olowa mu Ufumu wa zaka Chikwi chimodzi ndiponso mu Ufumu osatha wa Kumwamba, koma ochimwa amene sanakwanitse kutengako mbali mchiukitsochi choyamba adzakumana ndi chilango chachikulu cha mbale 7 chothilidwa ndi Mulungu ndi kuponyedwa mmoto osatha wa mgehena
Choncho, tsopano muyenera kuchokamo mu ziphunzitso zonse za chinyengo za zipembezo ndiponso mchilakolako ndi mu zinthu zosokonezeka za dzikoli, ndi kulowa mu Mawu oona a Mulungu. Ndikhulupilira ndi kupemphera kuti powerenga mndandanda wa ma uthenga anga a madzi ndi Mzimu, monse mdzaikidwa dalitso la machimo anu onse kuchotsedwa, ndi lolandira kubwera kwachiwiri kwa Ambuye athu kopanda mantha.

AUDIOBOOK
undefined
Due to COVID-19 and disruption to international mail service
we have temporally suspended our ‘Free Print Book service’.
In the light of this situation we are not able to mail you the books at this time.
Pray that this pandemic will end soon and the resumption of the postal service.