Chichewa 11

  • ㆍISBN : 9788928231775
  • ㆍPages : 253

Chikhupiliro Cha Chikhulupiro cha Atumwi - Mfundo Zenizeni Zoyambirira Pa za Khristu

Paul C. Jong

Ku ena aife amene okhulupilira mwa Mulungu, chikhulupiliro ndi zikhulupiliro za Atumwi zimatipatsa ziphunzitso zofunikira za uzimu. Chikhulupiliro chawo chimakhala chotilimbikitsa mmitima yathu, cifukwa iwo anakhulupilira mu uthenga umene umasunga chilungamo cha Mulungu. choncho, tonse mwamsanga tifunika kukhla ndi chikhulupiliro chotero.

Aliyense amene okhulupilira mwa Yesu ayenera kudziwa chiklungamo cha Mulungu ndi kukhulupilira mchimenecho, ndiponso iye ayenera kuufalitsa mdziko lonse, cifukwa ndipokhapo pamene ena naonso angadziwe chilungamocho ndi kukhulupilira mcimenecho. Ndiponso kupitila mu Mawu a Mulungu, ochimwa onse ayenera kuphunzira za chilungamo Chake. Ndipo ayenera kukhulupilira, pakuti umo ndi mmene angatengere chilungamo cha Mulungu mwa chikhulupiliro.

Kopanda chikhulupiliro cimene chimalora wina kupeza chilungamo cha Mulungu kuchokera mu Mawu Ake, palibe wina aliye amene angamvomere Ambuye ngati M'pulumutsi wake. Tsopano tiyenera kudziwa ndi kukhulupilira mu chilungamo cha Mulungu, pakuti ndi okhawo amene okhulupilira mu chilungamocho angakhale ansembe Ake omverera. Ansembe omumverera apa aimilira onse amene analandira chikhululukiro cha machimo awo pokhulupilira mu chilungamo cha Mulungu ndi kukhala anthu Ake olungama. Ndi chothekera kwambiri kwa onse aife kukhala ndi chikhulupiliro chofanana ndi Atumwi analinacho.

AUDIOBOOK
undefined
Due to COVID-19 and disruption to international mail service
we have temporally suspended our ‘Free Print Book service’.
In the light of this situation we are not able to mail you the books at this time.
Pray that this pandemic will end soon and the resumption of the postal service.