Chichewa 9

  • ㆍISBN : 9788928231843
  • ㆍPages : 378

Chihema: Chithunzi Chomasulira Mwatsatanetsatane za Yesu Kristu (Ⅰ)

Paul C. Jong

Kodi tingapedze motani coonadi co bitsala mu Cihema? Ndi pokhapo podzindikira uthenga wa madzi ndi Mzimu, ceni ceni ca Cihema, ndi pamene tingadziwe yankho ku funso limeneli.
Mcoonadi, nsaru zomwe zitaonekedwa pa kohomo la bwalo la Cihema limatisonyedza zincito za Yesu Kristu mu Cipangano ca Tsopano cimene cidapulumutsa anthu amudziko la pansi. Munjira yotere, Mau a mu Cipangano ca Kale ya mu Cihema ndi Mau a mu Cipangano ca Tsopano yali cimodzimodzi yo fanana, monga nsaru za mu Cihema. Koma, mwatsoka, ici coonadi cankhala cobitsika kwa nthgawi yaitali kwa iwo amene amafuna funa coonadi mu Ukristu.
Pobwera padziko lino, Yesu Kristu anabatizidwa ndi Yohane ndipo ana ketsa mwadzi Wace pa Mtanda. Kopanda kumvetsetsa ndi kukhulupirira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, palibe Umodzi waife yemwe anga dziwe coonadi cobvumbulutsidwa mu Cihema. Tiyenera kudziwa tsopano coonadi ici ca Chihema ndi kukhulupiriramo. Tonsefe tiyenera kudziwa ndi kukhulupirira mu coonadi coonekedwa nsaru zimene zitayalidwa pabwalo ya pakhomo ya Cihema.

AUDIOBOOK
undefined
Due to COVID-19 and disruption to international mail service
we have temporally suspended our ‘Free Print Book service’.
In the light of this situation we are not able to mail you the books at this time.
Pray that this pandemic will end soon and the resumption of the postal service.