Chichewa 16

  • ㆍISBN : 9788928239474
  • ㆍPages : 463

Ziphunzitso mu Agalatiya - Kuchoka Kumdulidwe wa Kuthupi Kufika Kuchiphunzitso Cha Kulapa (Ⅰ)

Paul C. Jong

Chiphunzitso cha Kulapa Ndichokwanira Kukupanhitsani kuti Mtore Matenda a Kuuzimu. .
Anthu mdziko lonse ali ndi mantha ndi tudoyo ngati SARS, cifukwa angafe mwamusanga mwa kuonetsedwa ku tudoyo totero tosaoneka.
Chimodzimodzi, Akristu masiku ano kudzungulira dziko lonse akufa mu mathupi awo ndiponso mu mzimu mwa kudwara ndi chiphunzitso cha kulapa. Kodi munali kudziwa kuti chiphunzitso cha kulapa ndi cholakwika moteromu?
Kodi mkudziwa amene anapangitsa Akristu kugwera mu dzenje lolowelera la chisokonezo cha mu mzimu. Ndi Akristu ochimwa iwo okha amene akupemphera mapemphero akulapa tsiku ndi tsiku kuti ayeretsedwe kumachimo awo a payekha payekha pamene akunena kuti okhulupilira mwa Yesu Khristu ngati M’pulumutsi wawo.
Chotero, muyenera kulandira chikhululukiro cha machimo mwa kukhulupilira mu Mawu a uthenga wa madzi ndi Mzimu umene Mulungu anatipatsa pachiyambi. Si muyenera kutaya mpata odalitsidwa okhala obadwa mwatsopano. Tonsefe tiyenera kumasulidwa kuchisokonezo cha mu mzimu mwa kukhulupilira mu Choonadi cha uthenga wa madzi ndi Mzimu. Tiyenera kuyangana pa kuwala konyezimira kwa Choonadi, cimene chinabwera kudzera mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, titathawako kunjira ya chisokonezo cha mu mzimu.

AUDIOBOOK
undefined
Due to COVID-19 and disruption to international mail service
we have temporally suspended our ‘Free Print Book service’.
In the light of this situation we are not able to mail you the books at this time.
Pray that this pandemic will end soon and the resumption of the postal service.