Chichewa 20

  • ㆍISBN : 9788928239771
  • ㆍPages : 407

Ziphunzitso pa Uthenga wa Yohane (Ⅲ) - Idyani Mnofu Wanga Ndiponso Imwani Magazi Anga

Paul C. Jong

Yesu Anatipatsa Moyo Osatha Kupitira mu Mnofu Wake ndi Magazi

M’pingo ukusunga masakalamenti awiri olamulidwa ndi Yesu. Oyamba ndi ubatizo, ndipo wina ndi Mgonero Oyera. Tikutengako mbali mu Mgonero kuti tilingalire pa Choonadi cha uthenga chovumvulutsidwa mu mkate wake ndi mu vinyo, mwa kukumbukira uthengau.
Mu chiphikiro cha Mgonero Oyera, tikudya mkate mwa kukhumbukira mnofu wa Yesu, ndipo tikumwa vinyo ngati chiphikiro cha magazi Ake. mwakutero, tanthauzo lenileni la Mgonero Oyera ndi kulimbikitsa chikhulupiliro chathu mu Choonadi chakuti Yesu anatipulumutsa kumachimo adziko ndipo anatipatsa moyo osatha kupitira mu ubatizo Wake ndi imfa Yake pa Mtanda.
Koma, bvuto ndi lakuti pafupi-fupi Akristu onse akutengako mbali mu Mgonero Oyera mwachizolowezi, kopanda ngakhalenso kuzindikira cimene Yesu anatanthauza ndi mawu, “Mnofu Wanga ndi chakudwadi, ndipo magazi Anga ndi chakumwa chenicehni” (Yohane 6:55). Chotero, mkati mwa uthenga wa madzi ndi Mzimu, tikuyenera kulingaliranso pa tanthauzo la Yesu kutilamula kuti tidye mnofu Wake ndi kumwa magazi Ake, ndi kukhulupilira m’menemo.

AUDIOBOOK
undefined
Due to COVID-19 and disruption to international mail service
we have temporally suspended our ‘Free Print Book service’.
In the light of this situation we are not able to mail you the books at this time.
Pray that this pandemic will end soon and the resumption of the postal service.