Chichewa 22

  • ㆍISBN : 9788928239979
  • ㆍPages : 474

Ziphunzitso pa Genesis (Ⅰ) - CHIFUNIRO Cha Utatu Oyera Ku Anthu

Paul C. Jong

Mu Buku la Genesis, cholinga cimene Mulungu anatilengera chikupezeka. Ngati omanga manyumba apanga maonekedwe a nyumba kapena olemba ailemba, poyamba akukhala ndi nchito imene adzakwanilitsidwa mu maganizo awo sanayambedi kugwira nchito pa nchito yawoyo. Momwemo, Mulungu wathu nayenso anali nacho chipulumutso chathu mu maganizo Ache cha anthu ngakhalenso asanalenge kumwamba ndi dziko lapansi, ndipo Iye anapanga Adamu ndi Eve mwa cholingachi mu maganizo. Mulungu anali kufuna kumasulira kwa ife a malo a Kumwamba, amene sakuoneka ndi maso athu a thupi, mwakupanga chifanizo cha malo a padziko lapansi cimene tonse tingachione ndi kuchimvetsetsa.
Ngakhalenso dziko lisanakhalepo, Mulungu anali kufuna kupulumutsa anthu mwa ngwiro mwa kuwapatsa uthenga wa madzi ndi Mzimu ku mtima wa munthu aliyense. Chotero ngakhale kuti anthu onse anapangidwa kuchoka kufumbi, ayenera kuphunzira ndi kudziwa Choonadi cha uthenga wa madzi ndi Mzimu kuti aphindulire miyoyo yawo. Ngati anthu akupitiliza kukhala kopanda kudziwa ulamuliro wa Kumwamba, adzataya osati zinthu zokha zadziko lapansi, komanso zinthu zonse zimene zili Kumwamba.

AUDIOBOOK
undefined
Due to COVID-19 and disruption to international mail service
we have temporally suspended our ‘Free Print Book service’.
In the light of this situation we are not able to mail you the books at this time.
Pray that this pandemic will end soon and the resumption of the postal service.