Chichewa 65

  • ㆍISBN : 9788928240876
  • ㆍPages : 397

KODI CHOFUNIKIRA NDI CHIANI KWA INU KUTI MUBADWENSO MWATSOPANO?

Paul C. Jong

Akristu lero ayenera kusintha maganizo ao. Iwo ayenera kukhulupilira mu Uthenga Wabwino wa madzi ndi Mzimu woperekedwa ndi Mulungu monga chipulumutso chao cheni cheni. Tonse tiyenera kuthokoza Ambuye potipatsa ife Uthenga umenewu Wabwino wa madzi ndi Mzimu. Kodi m’malo mwake tinganene bwanji kuti ntchito ya Ambuye ya chipulumutso yomwe yaombola ife ku machimo onse a dziko kuti ndiyolakwika? Kudzera m’bukuli pa Uthenga Wabwino wa madzi ndi Mzimu, ali yense tsopano ayenera kubadwa mwatsopano pokhulupilira muchipulumutso chomwe Ambuye wakwaniritsa kamodzi kokha. Ngati simukutsimikizabe za izi, muyenera kachiwiri kusinkhasinkha mwakuya pa chilungamo cha Mulungu chomwe Ambuye wapereka kwa inu.

AUDIOBOOK
Due to COVID-19 and disruption to international mail service
we have temporally suspended our ‘Free Print Book service’.
In the light of this situation we are not able to mail you the books at this time.
Pray that this pandemic will end soon and the resumption of the postal service.