Chichewa 1

  • ㆍISBN : 8983144599
  • ㆍPages : 437

KODI MWABADWADI MWATSOPANO MWA MADZI NDI MWA MZIMU?

Paul C. Jong

Ndime yamuthu waukhulu ya m'nkhaniyi ndi "ku Badwanso mwa Madzi ndi Mzimu." Muthuyu wachoka mnkhani yomweyi. Kunenetsa, bukuli likufothokoza tanthauzo lakubadwanso ndi mwamene mungabadwirenso mwa madzi ndi Mzimu mogwirizana ndi Bibulo. Madzi akuimirira ubadizo wa Yesu mu Yordani ndipo Babilo likuti machismo athu tonse anaikidwa pa Yesuyo pamene anabadizidwa ndi Yohane Mbatizi. Yohane ankhaimilira anthu amitundu yosina-siyana anali wambanja la Aloni wa Sembe Wamkhulu. Aloniyo aikha manja ake pa mbuzi yopepetsera machimo a Asiraeli achaka chonse Patsiku la Kupepetsera Machismo. Chinali chinthunzi-thunzi cha zinthu zabwino zikubwera. Kubadizidwa kwa Yesu kukufanizira kuikhapo manja kuja. Yesu anabadizidwa m'njira yoikha manja ku mtsinje wa Yordani uja. Ndiye anachotsa machismo adziko lonse paubadizo Wake ndipo anapachikidwa kuti alipe machimo athu. Koma anthu ambiri sakudziwa nchifukwa chanji Yesu anabadizidwa ndi Yohani mu Yordani. Ubadizo wa Yesu ndiyo nfundo yaikhulu mbukuli, imene singasiyanitsidwe ndi Uthenga wa Bwino wa madzi ndi Mzimu. Tingabadwenso ngati tikhulupirira mu ubadizo wa Yesu ndi Mtanda Wake.

Due to COVID-19 and disruption to international mail service
we have temporally suspended our ‘Free Print Book service’.
In the light of this situation we are not able to mail you the books at this time.
Pray that this pandemic will end soon and the resumption of the postal service.