Chichewa 2

  • ㆍISBN : 8983141417
  • ㆍPages : 321

BWELERANI KU UTHENGA WA MADZI NDI MZIMU

Paul C. Jong

Tiyeni tibwerere ku Uthenga wa madzi ndi Mzimu Woyera. Ziphunzitso ndi maphunziro a Mau a Mulungu sizingatipulumutse. Akhristu ambiri masiku ano ali kutsatilabe zimenezi ndipo sanabadwe mwatsopano. Buku ili litiuza momveka bwino zolakwika zimene zimapangidwa ndi ziphunzitso ndi maphunziro aza Mau a Mulungu ndiponso m’mene tingakhulupilire Yesu Khristu munjira yoyenera.
Due to COVID-19 and disruption to international mail service
we have temporally suspended our ‘Free Print Book service’.
In the light of this situation we are not able to mail you the books at this time.
Pray that this pandemic will end soon and the resumption of the postal service.