Chichewa 6

  • ㆍISBN : 8983143215
  • ㆍPages : 377

Chilungamo cha Mulungu Chimene Chinaululidwa mu Aroma - Ambuyathu anakhala chilungamo cha Mulungu (Ⅱ)

Paul C. Jong

Chilungamo Cha Mulungu chimaonekera ndipo chisiyana ndichija cha munthu. Chilungamo cha Mulungu chavumbulidwa muuthenga wamadzi ndi Mzimu, umene unakwaniritsidwa ndi kubadizidwa kwa Yesu kuli Yohane ndi mwazi Wake Pamtanda. Tibwerere kuchikhulupiliro cha Chilungamo cha Mulungu, tisachedwe.
Kodi ukudziwa ninji Yesu anabadizidwa ndi Yohne Mbadizi? Ngati Yohane sanabadize Yesu, machismo athu akanapatsidwa kwaiye. Yohane Mbadizi ndiye munthu wamkulu kupambana onse, ndipo ubadizo anapatsa Yesu unalingana ndichifuniro cha Mulungu kuti machismo athu apatsidwe kwa Yesu.
Yesu anabadizidwa kuti asenze machismo a anthu onse papewa pake, ndikufa pamtanda kulipa machismo. Zinthu zonsezi zasintha maganizo anga akuti kubadwanso nciani, chifukwa ndinangodziwa za mwazi pa Mtanda. Tsopano Mulungu wakupunzitsani kuti Chilungamo chake nhiani kuti tidziwe ndikukhulupilira mu Chilungamo chakecho mwatunthu. Ndithokoza Ambuye chifukwa chamadalitso onsewa.

AUDIOBOOK
undefined
Due to COVID-19 and disruption to international mail service
we have temporally suspended our ‘Free Print Book service’.
In the light of this situation we are not able to mail you the books at this time.
Pray that this pandemic will end soon and the resumption of the postal service.