Search

BUKU ELEKTRONIK DAN BUKU AUDIO GRATIS

Surat Rasul Paulus kepada Jemaat di Roma

Chichewa  5

Chilungamo cha Mulungu Chomwe Chaonetsedwa mu Aroma - Ambuye Wathu Yemwe Wakhala Chilungamo cha Mulungu (Ⅰ)

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928239856 | Halaman 467

Unduh buku elektronik dan buku audio GRATIS

Pilih format file yang Anda inginkan dan unduh dengan aman ke perangkat seluler, PC, atau tablet Anda untuk membaca dan mendengarkan kumpulan khotbah kapan saja dan di mana saja. Semua buku elektronik dan buku audio sepenuhnya gratis.

Anda dapat mendengarkan buku audio melalui pemutar di bawah ini. 🔻
Miliki buku cetak
Beli buku cetak di Amazon
Zamkatimu
 
Mau Oyamba 

MUTU 1 
1. Mau Oyamba kwa Aroma Mutu 1 
2. Chingamo cha Mulungu Chimene Chaonetsedwa mu Uthenga Wabwino (Aroma 1:16-17) 
3. Wolungama adzakhala ndi moyo ndi chikhulupiliro (Aroma 1:17) 
4. Wolungama Amakhala ndi Moyo ndi Chikhulupiliro (Aroma 1:17-18) 
5. Iwo amene Akukanikiza Pansi Choonadi mu Chosalungama (Aroma 1:18-25) 

MUTU 2 
1. Mau Oyamba kwa Aroma Mutu 2 
2. Iwo Amene Amanyalanyaza Chisomo cha Mulungu (Aroma 2:1-16) 
3. Mdulidwe Uli wa Mtima (Aroma 2:17-29) 

MUTU 3 
1. Mau Oyamba kwa Aroma Mutu 3 
2. Chipulumutso ku Machimo mwa Chikhulupiliro Chokha (Aroma 3:1-31) 
3. Kodi Mumathokoza Mulungu Chifukwa cha Ambuye? (Aroma 3:10-31) 

MUTU 4 
1. Mau Oyamba kwa Aroma Mutu 4 
2. Iwo Amene Analandira Madalitso a Kumwamba ndi Chikhulupiliro (Aroma 4:1-8) 

MUTU 5 
1. Mau Oyamba kwa Aroma Mutu 5 
2. Kudzera mwa Munthu Mmodzi (Aroma 5:14) 

MUTU 6 
1. Mau Oyamba kwa Aroma Mutu 6 
2. Tanthauzo Lenileni la Ubatizo wa Yesu (Aroma 6:1-8) 
3. Perekani Ziwalo Zanu Zikhale Zida za Chilungamo (Aroma 6:12-19) 
 
Uthenga wa Madzi ndi Mzimu N’chilungamo cha Mulungu!
Mawu a mu bukuli akupha ludzu m,mtima wanu. Akristu a masiku ano akupitiliza kukhala ndi moyo pamene sakudziwa yankho lenileni la machimo enieni amene akuchita tsiku ndi tsiku. Kodi mkuchidziwa chimene n’chilungamo cha Mulungu? Ndikhulupilira kuti mdzazifunsa nokha funsoli ndi kukhulupilira mu chilungamo cha Mulungu, chimene chikuululidwa mu bukuli.
Chilungamo cha Mulungu chakhala ndi uthenga wa madzi ndi Mzimu. Koma, ngati chuma cha mtengo wapatali, chasungidwa mobisika ku maso amene akusatira zazipempbezo kwa nthawi yaitali. Ngati zotulukamo zake, anthu ambiri anadalira pa chimenecho ndi kuzikuza cifukwa cha chilungamo chawo m’malo mwa kukhulupilira mu chilungamo cha Mulungu. Chotero, ziphunzitso za Chikristu zimene si zikupanga ngakhalenso ziganizo zolongosoka zinakhala zikhulupiliro zolamulira m’mitima ya okhulupilira, ngati n’paja ziphunzitsozi zili ndi chilungamo cha Mulungu.
ziphunzitso za Kusankhidwa, Kuyeretsedwa, ndiponso Kusukidwa mwa pang’onopang’ono ndi ziphunzitso zadzikulu za Chikristu, zimene zinabweretsa msokonezo ndi kupanda kanthu m’miyoyo ya okhulupilira. Koma tsopano, Akristu ambiri ayenera kudziwa Mulungu mwatsopano, aphunzire za chilunamo Chake ndipo apitilize kukhala mu chikhulupiliro chosimikizidwa.
"Ambuyathu amene anakhala chilungamo cha Mulungu” adzapatsa moyo wanu kumvetsetsa kwakukulu ndi kuwotsogolera ku mtendere. Mlembi akufuna kuti inu mkhale nalo dalitso la kudziwa chilungamo cha Mulungu. Dalitso la Mulungu likhale nanu!
 
Lebih
Pemutar buku audio

Buku-buku yang terkait dengan judul ini

The New Life Mission

Bagaimana Anda mengetahui tentang kami?

Bagaimana Anda mengetahui tentang kami?