Cărți creștine gratuite pentru studii biblice despre mântuire, Duhul Sfânt,
Cortul și Apocalipsa lui Ioan

Acasă  |  Harta site-ului  |  Contact  |  Ajutor    
Studii biblice Cărți creștine gratuite cărți electronice creștine gratuite Despre noi
  Versiune de carte electronică GRATUITĂ a ediției 5 în limba Chichewaneză

 


Ambuyathu anakhala chilungamo cha Mulungu (I)

- Chilungamo cha Mulungu Chimene Chinaululidwa mu Aroma

 • Format de carte electronică : Acrobat PDF Reader
 • Descărcări curente : 2
 • Despre această carte
 • Tabela de conținut
 

Kulengeza:

Chilungamo cha Mulungu Chimene Chinaululidwa mu Aroma.

Kufothokoza:

Uthenga wa Madzi ndi Mzimu N’chilungamo cha Mulungu!

Mawu a mu bukuli akupha ludzu m,mtima wanu. Akristu a masiku ano akupitiliza kukhala ndi moyo pamene sakudziwa yankho lenileni la machimo enieni amene akuchita tsiku ndi tsiku. Kodi mkuchidziwa chimene n’chilungamo cha Mulungu? Ndikhulupilira kuti mdzazifunsa nokha funsoli ndi kukhulupilira mu chilungamo cha Mulungu, chimene chikuululidwa mu bukuli.
Chilungamo cha Mulungu chakhala ndi uthenga wa madzi ndi Mzimu. Koma, ngati chuma cha mtengo wapatali, chasungidwa mobisika ku maso amene akusatira zazipempbezo kwa nthawi yaitali. Ngati zotulukamo zake, anthu ambiri anadalira pa chimenecho ndi kuzikuza cifukwa cha chilungamo chawo m’malo mwa kukhulupilira mu chilungamo cha Mulungu. Chotero, ziphunzitso za Chikristu zimene si zikupanga ngakhalenso ziganizo zolongosoka zinakhala zikhulupiliro zolamulira m’mitima ya okhulupilira, ngati n’paja ziphunzitsozi zili ndi chilungamo cha Mulungu.
ziphunzitso za Kusankhidwa, Kuyeretsedwa, ndiponso Kusukidwa mwa pang’onopang’ono ndi ziphunzitso zadzikulu za Chikristu, zimene zinabweretsa msokonezo ndi kupanda kanthu m’miyoyo ya okhulupilira. Koma tsopano, Akristu ambiri ayenera kudziwa Mulungu mwatsopano, aphunzire za chilunamo Chake ndipo apitilize kukhala mu chikhulupiliro chosimikizidwa.
"Ambuyathu amene anakhala chilungamo cha Mulungu” adzapatsa moyo wanu kumvetsetsa kwakukulu ndi kuwotsogolera ku mtendere. Mlembi akufuna kuti inu mkhale nalo dalitso la kudziwa chilungamo cha Mulungu. Dalitso la Mulungu likhale nanu!


Mau a wosindikiza:

Mlembi wa bukuli ndiye oyambitsa wa New Life Mission ndipo wakhala akulalikira mawu a madzi ndi Mzimu, amene ali ndi chilungamo cha Mulungu, kudzugulira dziko lonse. Nchito zake, zimene tsopanoli zamasulidwa mu zinenero 50 zazikulu zikulu, zikugawidwa ku maiko opitilira pa 150. Anthu onse kudzungulira dziko lonse angalandire dalitso lalikulu lakupeza chilungamo cha Mulungu kudzera mu mawu a Mulungu, amene Reverend Jong akulalika limodzi ogwira nawo nchito anzake. Kodi cifukwa n’chiyani si mungalandire chikhululukiro cha machimo ndipo mkonzekera za moyo wanu osatha mwa kukhulupilira mu mawa a Mulungu kudzera mu ziphunzitso za bukuli?


  Trimite prin email această pagină de site unui prieten

 
Free Christian eBooks
    Lista de cărți electronice
    Chichewaneză ediția 5
 
 • Despre această carte
 •  
 • Tabela de conținut
 •     Ce este o carte electronică ?
   
 • Despre cartea electronică
 •  
 • Cum să citești o carte electronică ?
 •  
 • ÎFP
 •  
 • Ajutor pentru descărcare
 •     Cititori ai cărții electronice
   
 • MS Reader 2.0
 •  
 • Acrobat Reader 4.0
 •  

     
  Copyright © 2001 - 2019 The New Life Mission. ALL RIGHTS reserved.