Chichewa 23

  • ㆍISBN : 9788928240050
  • ㆍPages : 362

Ziphunzitso pa Genesis (Ⅱ) - Kugwa kwa Munthu ndi Chipulumutso Cholungama cha Mulungu

Paul C. Jong

Mu Buku la Genesisi, cholinga cha cimene Mulungu anatilengera chipezeza. Pamene architekicha alemba nyumba kapena wolemba adinda chithunzi, poyamba amayamba akhala ndi nchito ija imene angakwanilitsidwe mu maganizo yawo sanayambe kugwira nchito pa polonjekiti yawo. Monga chotero, Mulungu nayenso anali ndi chipulumutso chathu mu maganizo Ake ngakhale Iye asanalenge kumwamba ndi dziko lapansi, ndipo anapanga Adamu ndi Hava mu cholinga Chake cha mu maganizo. Ndipo Mulungu anafotokoza za malo a Kumwamba, amene samaoneka ndi maso athu a thupi, polemba mndandanda wa malo apadziko lapansi amene tingayaone tonse ndi kumvesetsa.
Ngakhale kuchokera pamaziko ya dziko, Mulungu anali kufuna kupulumutsa anthu molungama popereka uthenga wa madzi ndi Mzimu ku mtima wa aliyense. Kotero ngakhale anthu onse anapangidwa kuchokera kufumbi, ayenera kuphunzira ndi kudziwa Choonadi cha uthenga wa madzi ndi Mzimu kuti miyoyo yawo yisangalale. Anthu akapitiriza kukhala opanda kudzindikira mphamvu za Kumwamba, adzataya zinthu osati za padziko lapansi zokha, komaso ndi zonse za Kumwamba.

Audiolibros
undefined
Debido a COVID-19 y la interrupción del servicio de correo internacional,
hemos suspendido temporalmente nuestro "Servicio de Libros Impresos Gratis".
A la luz de esta situación no podemos enviarle los libros por correo en este momento.
Oren para que esta pandemia termine pronto y por la reanudación del servicio postal.