Chichewa 53

  • ㆍISBN : 9788928240777
  • ㆍPages : 422

NZERU YA UTHENGA WABWINO WAKALE

Paul C. Jong

Uthenga Wabwino wakale otchulidwa m’buku ili ndi Uthenga Wabwino oyamba otchedwa kuti “Uthenga Wabwino wa madzi ndi Mzimu.” Mpaka pano, komabe, Akristu ambiri sakudziwa kuti Uthenga Wabwino wa madzi ndi Mzimu ndiye Uthenga Wabwino oyamba, ndipo zotsatira zake akhulupilira molakwika mu ‘Uthenga wa hafu’. Ndi chifukwa chake chikhulupiliro chao sichipita patali, ndipo zakhala zosatheka kwa iwo kuona kukula mu uzimu. Chikhulupiliro chao chakhala choperewera nthawi zonse, chodzadza ndi malamulo kapena chikhulupiliro cha zinsinsi. Zotsatira zake sangadzithandize okha koma kukhala ndi mitima yochimwa. Kodi ndi mphamvu yanji ya uzimu yomwe Akristu otere angakhale nayo pamene adakali ndi machimo m’mitima yao? Chifukwa akhala Akristu opanda mphamvu, myoyo yao mu dziko lino ilibenso ntchito. Tinganene tsopano kuti Akristu alero ali ndi Uthenga wa hafu kuyambira pa nthawi yomwe mpingo oyamba unatha. Motero, tonse a ife tiyenera kuzindikiranso Uthenga Wabwino wakale tsopano nthawi isanathe, dziwani chikondi cha Mulungu choonadi ndi kukhulupilira mu chikondi choonadichi.

Audiolibros
Debido a COVID-19 y la interrupción del servicio de correo internacional,
hemos suspendido temporalmente nuestro "Servicio de Libros Impresos Gratis".
A la luz de esta situación no podemos enviarle los libros por correo en este momento.
Oren para que esta pandemia termine pronto y por la reanudación del servicio postal.