Chichewa 3

  • ㆍISBN : 8983141069
  • ㆍPages : 361

Mzimu Woyera Amene Akukhala mwa Ine -Njira Yodalirika yakuti Inu Mulandiliremo Mzimu Woyera

Paul C. Jong

Mchikristu cha masiku ano, nkhani zokambilana zambiri ndi “chipulutso ku uchimo” ndi “kukhala kwa Mzimu Woyera.” Koma, ndi anthu ochepa amene ali ndi nzeru yeniyeni ya mfundo ziwirizi, ngakhale choona ndi chakuti zinthu ziwiri n’zofunikira mfundo za Chikristu. Chimene chikuoopsa kwambiri, sitingapeza cholemba cha mu baibulo chilichonse chimene chikutiphunzitsa molondola za nkhani za pamwambapa. Kunali alembic ambiri a zachikristu kulemekeza mphatso za Mzimu Woyera kapena kufotokoza miyoyo yodzadza ndi Mzimu. Koma palibe wina aliyense wa iwo amene akuyetsa kuthana ndi funso lenileni, “Kodi okhulupilira angalandiredi motani Mzimu Woyera?” Kodi chifukwa n’chiyani? Choonadi chodabwitsa ndi chakuti sanalembepo za ichi mozama chifukwa alibe nzeru yeniyeni ya zachimenechi. Monga m’mene Mneneri Hoseya anafuura, “Anthu anga akuonongeka chifukwa akusowa nzeru,” masiku ano, palibe ngakhale Akristu ochepa amene sakutengedwera mu chipembezo chotentheka, kuyembekezera kulandira Mzimu Woyera. Iwo akukhulupira kuti adzalandira Mzimu Woyera mwa kufika pakaonekedwe kakufunitsitsa ndi kamisala. Koma sikulongola kunena kuti chotchedwa chikhulupiliro chawo chikubwezera Chikristu mu matsenga wamba, ndi kuti kutentheka kotere kukuchokera kwa Satana.
Mlembi Rev. Paul C. Jong akufuna kulengeza choonadi. Iye akuthana ndi mutu ofunikira mozama, umene alembe ambiri auzimu auzemba kwa nthawi yaitali. Iye poyamba akumasulira tanthauzo la “kubadwa mwatsopano” ndi “kukhala kwa Mzimu Woyera,” ndipo akumasulira mgiwirizona osaleketsedwa pakati pa mfundo zapakati ziwirizi. Kenako iye akutsogolera ndondomeko yonse ya kufotokoza kokhuzana ndi Mzimu Woyera, kuyambira, “m’mene mngadziwire mizimu,” mpaka “kunjira ya miyoyo yodzala ndi Mzimu.” Kuti mdziwe zambiri , mlembi akukulimbikitsani kuti muyeze zamkati mwa bukuli loikidwa pa webisaitiyi.

Audiolibros
NY/03/Ch01_Mzimu Woyera Umagwira Nchito Mkati mwa Mawu a Mulungu a Lonjezo.mp3
Debido a COVID-19 y la interrupción del servicio de correo internacional,
hemos suspendido temporalmente nuestro "Servicio de Libros Impresos Gratis".
A la luz de esta situación no podemos enviarle los libros por correo en este momento.
Oren para que esta pandemia termine pronto y por la reanudación del servicio postal.