Search

БЕЗКОШТОВНІ ЕЛЕКТРОННІ КНИГИ ТА АУДІОКНИГИ

Лист апостола Павла до ефесян

Чичева  27

Ziphunzitso pa Aefeso (I) - CIMENE MULUNGU AKULANKHULA KWA IFE KUPITIRA MU KALATA WA KU AEFESO

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928240135 | Сторінки 477

Завантажте електронні книги та аудіокниги БЕЗКОШТОВНО

Виберіть бажаний формат файлу та безпечно завантажте на мобільний пристрій, ПК або планшет, щоб читати та слухати колекції проповідей будь-де та будь-коли. Всі електронні книги та аудіокниги повністю безкоштовні.

Ви можете прослухати аудіокнигу через плеєр нижче. 🔻
Майте друковану книгу
Купіть друковану книгу на Amazon
Zamkati
 
Mawu Oyamba 
Mawu a Chikumbutso Ochokera kwa Mlembi 
 
1. Kodi Ana a Mulungu Anakhalako Motani? (Aefeso 1:1-23) 
2. Kodi Wauzimu Pamaso pa Mulungu N’ndani? (Aefeso 1:1-14) 
3. Kodi M’pingo wa Mulungu Ndichiyani ? (Aefeso 1:23) 
4. Chilungamo Cha Yesu Khristu Chimene Chidzala Zinthu Zonse Mokwanira (Aefeso 1:20-23) 
5. Kodi Mulungu Anatipulumutsadi mwa Chisomo Chake? (Aefeso 2:1-5) 
6. Yesu Ndiye Mtendere Wathu (Aefeso 2:14-22) 
7. Yesu Anagwetsa Khoma La Uchimo Limene Linatilekanitsa kwa Mulungu (Aefeso 2:11-22) 
8. Kodi Tikukhala Moyamikira Mwa Kukhulupilira mu Uthenga wa Madzi ndi Mzimu? (Aefeso 2:1-7) 
9. Gwirani Nchito Yanu Yauzimu Mosalekeza (Aefeso 3:1-21) 
10. Chikondi cha Khristu chili mu Mtima mwa Oyera Aliyense (Aefeso 3:14-21) 
11. Khalani Umoyo Wanu wa Chikhulupiriro Mwa Chikhulupiriro Chimodzi Ndiponso Cholinga Chimodzi (Aefeso 4:1-6) 
12. Tinavala Chisomo cha Khristu (Aefeso 4:1-16) 
13. Ndi Dalitso Kwambiri Kwa Ife Kuthandizira Utumiki Wa Uthenga! (Aefeso 5:1-17) 
14. Ubale Pakati pa Mulungu ndi M’pingo Wake (Aefeso 5:22-33) 
15. Kutumikira Ambuye ndi Njira Yakudzazidwa ndi Mzimu Woyera (Aefeso 5:18-21) 
16. Tumikiranani Wina ndi Mzake Monga M’mene Mkutumikira Khristu (Aefeso 6:1-9) 
 
Kodi Mkudziwa M’mene Ulili M’pingo wa Mulungu?

Mwa kukhulupilira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, muyenera kukhala ndi maso anu akuuzimu masiku onse otseguka. Ngati munalandira chikhululukiro cha machimo anu mwa kukhulupilira moona mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, ndiye kuti mdzatha kuzindikira M'pingo wa Mulungu moyenera; apo bii, simukanatha kudziwa moyenera imene ndi mipingo yaboza.
Masiku ano, Mulungu anakhazikitsa M'pingo Wake pachikhulupiliro cha okhulupilira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu. M'pingo wa Mulungu ndi kusonkhana kwa aja amene anapulumutsidwa mwa kukhulupilira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu. Chotero, ngati mitima yanu tsopano ili ndi chikhulupiliro mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, ndiye kuti kenako mungakhale ndi chikhulupiliro mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, kenako mungakhale moyo woona wachikhulupiliro. Moyo otero wachikhulupiliro ndi wotheka mu M'pingo wa Mulungu mokha. Moonjezera, chikhulupiliro chotere chokha chikutiyeneretsa kukakhala kwa muyaya mu Ufumu wa Ambuye. Kupitira muchikhulupiliro ichi, tiyenera kulandira chikondi cha chipulumutso ndi madalitso onse auzimu a Kumwamba kuchokera kwa Mulungu Atate, kwa Yesu Khristu, ndi ku Mzimu Woyera.
Більше

Книги, схожі на цю

The New Life Mission

зьміть участь у нашому опитуванні

Як ви дізналися про нас?