• 所有新生命宣教会 The New Life Mission 网站上的电子书和有声书均可免费下载
  • 探索以多种语言提供的全球性讲道
  • 查看我们已翻译成27种语言的网站
  • 第1卷新修订版已全新推出
Search

免费电子书和有声读物

使徒保罗写给罗马人的书信

奇切瓦语  6

Chilungamo cha Mulungu Chomwe Chaonetsedwa mu Aroma - Ambuye Wathu Yemwe Wakhala Chilungamo cha Mulungu (Ⅱ)

Rev. Paul C. Jong | ISBN 8983143215 | 页码 377

下载免费电子书和有声读物

选择您喜欢的文件格式,安全下载到手机、电脑或平板电脑,随时随地阅读和收听讲道集。所有电子书和有声读物都完全免费。

您可以通过下方播放器收听有声读物。🔻
Zamkatimu
 
Mau Oyamba 

Mutu 7
1. Mau Oyamba kwa Aroma Mutu 7 
2. Mfundo ya Chikhulupiliro cha Paulo: Kulumikizana ndi Kristu titafa ku uchimo (Aroma 7:1-4) 
3. Chifukwa Chomwe Tingatamandire Ambuye (Aroma 7:5-13) 
4. Thupi lathu Lomwe Limatumikira Thupi Lokha Basi (Aroma 7:14-25) 
5. Thupi Limatumikira Lamulo la Uchimo (Aroma 7:24-25) 
6. Tamandani Ambuye, Mpulumutsi wa Ochimwa (Aroma 7:14-8:2) 

Mutu 8
1. Mau Oyamba kwa Aroma Mutu 8 
2. Chilungamo cha Mulungu, Chikwaniritso cha Chofunikira Cholungama cha Lamulo (Aroma 8:1-4) 
3. Kodi m’Kristu Ndindani? (Aroma 8:9-11) 
4. Chisamaliro cha Thupi chiri Imfa, koma Chisamaliro cha Mzimu chiri Moyo ndi Mtendere (Aroma 8:4-11) 
5. Kuyenda mu Chilungamo cha Mulungu (Aroma 8:12-16) 
6. Iwo amene amalowa Ufumu wa Mulungu (Aroma 8:16-27) 
7. Kubwera Kwachiwiri kwa Ambuye komanso Ufumu wa Zakachikwi (Aroma 8:18-25) 
8. Mzimu Woyera Umene Umathandiza Olungama (Aroma 8:26-28) 
9. Zinthu Zonse Zithandizana Kuwachitira Ubwino (Aroma 8:28-30) 
10. Ziphunzitso Zolakwika (Aroma 8:29-30) 
11. Chikondi Chosatha (Aroma 8:31-34) 
12. Ndindani Angayese Kutsutsana Nafe? (Aroma 8:31-34) 
13. Ndindani Amene Adzasiyanitsa Olungama ku Chikondi cha Kristu? (Aroma 8:35-39) 

Mutu 9
1. Mau Oyamba kwa Aroma Mutu 9 
2. Tiyenera Kudziwa Kuti Kukonzedweratu Kunakonzedwa Mkati mwa Chilungamo cha Mulungu (Aroma 9:9-33) 
3. Kodi ndi kulakwitsa Mulungu Kukonda Yakobo? (Aroma 9:30-33) 

Mutu 10
1. Mau Oyamba kwa Aroma Mutu 10 
2. Chikhulupiliro Chenicheni Chidza ndi Mbiri (Aroma 10:16-21) 

Mutu 11
1. Kodi Israyeli Adzapulumutsidwa? 

Mutu 12
1. Konzani Mtima Wanu Pamaso pa Mulungu 

Mutu 13
1. Khalani Chifukwa cha Chilungamo cha Mulungu 

Mutu 14
1. Musaweruzane Wina ndi Mnzake 

Mutu 15
1. Tiyeni Tifalitse Uthenga Wabwino ku Dziko Lonse Lapansi 

Mutu 16
1. Mulankhulane Wina ndi Mnzake 
 
Chilungamo Cha Mulungu chimaonekera ndipo chisiyana ndichija cha munthu. Chilungamo cha Mulungu chavumbulidwa muuthenga wamadzi ndi Mzimu, umene unakwaniritsidwa ndi kubadizidwa kwa Yesu kuli Yohane ndi mwazi Wake Pamtanda. Tibwerere kuchikhulupiliro cha Chilungamo cha Mulungu, tisachedwe.
Kodi ukudziwa ninji Yesu anabadizidwa ndi Yohne Mbadizi? Ngati Yohane sanabadize Yesu, machismo athu akanapatsidwa kwaiye. Yohane Mbadizi ndiye munthu wamkulu kupambana onse, ndipo ubadizo anapatsa Yesu unalingana ndichifuniro cha Mulungu kuti machismo athu apatsidwe kwa Yesu.
Yesu anabadizidwa kuti asenze machismo a anthu onse papewa pake, ndikufa pamtanda kulipa machismo. Zinthu zonsezi zasintha maganizo anga akuti kubadwanso nciani, chifukwa ndinangodziwa za mwazi pa Mtanda. Tsopano Mulungu wakupunzitsani kuti Chilungamo chake nhiani kuti tidziwe ndikukhulupilira mu Chilungamo chakecho mwatunthu. Ndithokoza Ambuye chifukwa chamadalitso onsewa.
更多
有声书播放器

与该标题相关的书籍

The New Life Mission

参加我们的调查

您是如何了解到我们的?