• 所有新生命宣教会 The New Life Mission 网站上的电子书和有声书均可免费下载
  • 探索以多种语言提供的全球性讲道
  • 查看我们已翻译成27种语言的网站
  • 第1卷新修订版已全新推出
Search

免费电子书和有声读物

启示录

奇切瓦语  7

Ndemanga ndi Ulaliki pa Buku la Chibvumbulutso - KODI NYENGO YA WOTSUTSAKRISTU, KUFERA CHIKHULUPILIRO, MKWATULO KOMANSO UFUMU WA ZAKACHIKWI IKUDZA? ( I )

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928231294 | 页码 369

下载免费电子书和有声读物

选择您喜欢的文件格式,安全下载到手机、电脑或平板电脑,随时随地阅读和收听讲道集。所有电子书和有声读物都完全免费。

您可以通过下方播放器收听有声读物。🔻
拥有平装书
在亚马逊购买平装书
Zamkatimu 
 
Mau Oyamba 

MUTU 1
1. Imvani Mau a Chibvumbulutso cha Mulungu (Civumbulutso 1:1-20) 
2. Tiyenera Kudziwa Nyengo Zisanu Ndi Ziwiri 

MUTU 2
1. Kalata ya Mpingo wa ku Efeso (Chivumbulutso 2:1-7) 
2. Chikhulupiliro Chomwe Chingalandire Kuphedwa Chifukwa cha Kristu 
3. Kalata ya Mpingo wa ku Smurna (Chibvumbuutso 2:8-11) 
4. Khalani Okhulupirika kufikira Imfa 
5. Ndindani Wopulumutsidwa ku Uchimo? 
6. Kalata ya Mpingo wa ku Pergamo (Chibvumbulutso 2:12-17) 
7. Osatira Chiphunzitso cha Anikolai 
8. Kalata ya Mpingo wa ku Tiyatira (Chibvumbulutso 2:18-29) 
9. Kodi Mwapulumutsidwa mwa Madzi ndi Mzimu? 

MUTU 3
1. Kalata ya Mpingo wa ku Sarde (Chibuvumbulutso 3:1-6) 
2. Iwo Amene Sanadetse Zobvala Zao Zoyera 
3. Kalata ya Mpingo wa ku Filadelfeya (Chibvumbulutso 3:7-13) 
4. Akapolo komanso Oyera Mtima a Mulungu Omwe Amakondweretsa Mtima Wake 
5. Kalata Ya Mpingo wa ku Laodikaya (Chibvumbulutso 3:14-22) 
6. Chikhulupiliro Choona cha Moyo wa Ophunzira 

MUTU 4
1. Onani Yesu Yemwe Wakhala pa Mpando Wachifumu wa Mulungu (Chibvumbulutso 4:1-11) 
2. Yesu ndi Mulungu (Chibvumbulutso 4:1-11) 

MUTU 5 
1. Yesu Amene Waikidwa pa Mpando Wachifumu monga Woimilira wa Mulungu Atate (Chibvumbulutso 5:1-14) 
2. Mwanawankhosa Yemwe Wakhala pa Mpando Wachifumu 

MUTU 6
1. Nyengo Zisanu ndi Ziwiri Zoikidwa ndi Mulungu (Chibvumbulutso 6:1-17) 
2. Nyengo za Zisindikizo Zisanu ndi Ziwiri 

MUTU 7
1. Ndindani Amene Adzapulumutsidwa mu Nthawi ya Chisautso Chachikulu? (Chibvumbulutso 7:1-17) 
2. Tiyeni Tikhale Ndi Chikhulupiliro Chomwe Chimamenya Nkhondo (Chibvumbuluitso 7:1-17) 
 
Chitapita chipolowe chazigewenga cha 9/11, mafunso ku “www.raptureready.com” Intaneti saiti pankhani ya nyengo, anachulukira kufika ku mamiliyoni opitilira ku 8 anafika, malinga ndi kafuku-fuku wa CNN ndi TIME, ma Ameleka opitilira pa 59% akhulupilira mkukwatula kosilizira.
Kunena za nyengo, mlembiyu akunena mfundo zeni-zeni za mutu wa buku la Chivumbulutso, kunenanso zakubwera kwa Wosusa Khristu, kuphedwa kwa oyera ndikukwatulidwa kwao, Ufumu wa zaka Chikwi chimodzi, ndi Kumwamba kwa Tsopano ndi Dziko la tsopano-zonse kulingana ndi Malembo wonse ndiponso motsogoleledwa ndi Mzimu Woyera.
Bukuli limapatsa ndemanga za ndime ndi ndime mu Buku la Chuvumbulutso powonjezedwa ndi ziphunzitso zozama za mlembi. Aliyense amene amawerenga bukuli adzadziwa zolinga zonse zimene Mulungu anasungira dzikoli lapansi.
Tsopano ndi nthawi kuti inu mdzindikire chofunikira cheni-cheni mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, kotero kuti mupeze nzeru zimene zingakuomboleni kuchoka ku mayetsero onse ndi masautso a nthawi yamapeto. Ndi mabukuwa awiri, ndiponso pokhulupilira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, mdzakwanitsa kupambana mayetsero onse ndi masautso ananeneredwa mu Chivumbulutso.
更多
有声书播放器

与该标题相关的书籍

The New Life Mission

参加我们的调查

您是如何了解到我们的?