• 所有新生命宣教会 The New Life Mission 网站上的电子书和有声书均可免费下载
  • 探索以多种语言提供的全球性讲道
  • 查看我们已翻译成27种语言的网站
  • 第1卷新修订版已全新推出
Search

免费电子书和有声读物

使徒保罗写给加拉太的书信

奇切瓦语  16

Ziphunzitso mu Agalatiya - Kuchoka Kumdulidwe wa Kuthupi Kufika Kuchiphunzitso Cha Kulapa (Ⅰ)

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928239474 | 页码 463

下载免费电子书和有声读物

选择您喜欢的文件格式,安全下载到手机、电脑或平板电脑,随时随地阅读和收听讲道集。所有电子书和有声读物都完全免费。

您可以通过下方播放器收听有声读物。🔻
拥有平装书
在亚马逊购买平装书
Zamkati
 
Kalambulabwalo 

CHAPITALA 1
1. Ambuye Anatilanditsa Kudzikoli Loipa (Galatiya 1:1-5) 
2. Kodi Chikhulupiliro Chanu Sichili Chofanana ndi Cha Amudulidwe Mwina? (Galatiya 1:1-5) 
3. Ambuye Anatilanditsa Mwa Ungwiro ndiponso Mwa Kamodzi Kokha (Galatiya 1:3-5) 
4. Sipangakhalenso Uthenga Wina Koma Uthenga wa Madzi ndi Mzimu (Galatiya 1:6-10) 
5. Aja Amene Mitima Yawo Inaikidwa Ngati Atumiki a Mulungu (Galatiya 1:10-12) 
6. Chikhulupiliro Cha Mtumwi Paulo Ndi Chenjezo Lake ku Amudulidwe (Galatiya 1:1-17) 
7. Moyo Wachikhulupiriro Chachilamulo Ubweretsa Matemberero Okha (Galatiya 1:1-24) 

CHAPITALA 2
1. Chifukwa N’chiyani Mtumwi Paulo Anasura a Zachilamulo? (Galatiya 2:1-10) 
2. Tanthauzo Leni-leni la Chikhulupiliro cha Paulo (Galatiya 2:20) 
3. Mwachikhulupiliro mu Mwana wa Mulungu, Kodi Tinafa ndi Kuukitsidwa Limodzi Ndi Iye? (Galatiya 2:20) 
4. Munthu Samayetsedwa Olungama ndi Nchito za Chilamulo Koma mwa Chikhulupiliro mu Uthenga wa Madzi ndi Mzimu (Galatiya 2:11-21) 
5. Tikuyetsedwa Wolungama mwa Chikhulupiliro Choyera Chokha (Galatiya 2:11-21) 

CHAPITALA 3
1. Masiku Onse Khalani Moyo wanu Mwa Chikhulupiliro mu Uthenga wa Madzi ndi Mzimu (Galatiya 3:1-11) 
2. Kodi Kupanda Kanthu kwa Mitima Yathu Kukuzimiririka Nthawi Yotani? (Galatiya 3:23-29) 
3. Tsopano Sitiyenera Kukhalanso Pansi pa Matembelelo a Chilamulo (Galatiya 3:1-29) 
 
Chiphunzitso cha Kulapa Ndichokwanira Kukupanhitsani kuti Mtore Matenda a Kuuzimu.

Anthu mdziko lonse ali ndi mantha ndi tudoyo ngati SARS, cifukwa angafe mwamusanga mwa kuonetsedwa ku tudoyo totero tosaoneka.
Chimodzimodzi, Akristu masiku ano kudzungulira dziko lonse akufa mu mathupi awo ndiponso mu mzimu mwa kudwara ndi chiphunzitso cha kulapa. Kodi munali kudziwa kuti chiphunzitso cha kulapa ndi cholakwika moteromu?
Kodi mkudziwa amene anapangitsa Akristu kugwera mu dzenje lolowelera la chisokonezo cha mu mzimu. Ndi Akristu ochimwa iwo okha amene akupemphera mapemphero akulapa tsiku ndi tsiku kuti ayeretsedwe kumachimo awo a payekha payekha pamene akunena kuti okhulupilira mwa Yesu Khristu ngati M’pulumutsi wawo.
Chotero, muyenera kulandira chikhululukiro cha machimo mwa kukhulupilira mu Mawu a uthenga wa madzi ndi Mzimu umene Mulungu anatipatsa pachiyambi. Si muyenera kutaya mpata odalitsidwa okhala obadwa mwatsopano. Tonsefe tiyenera kumasulidwa kuchisokonezo cha mu mzimu mwa kukhulupilira mu Choonadi cha uthenga wa madzi ndi Mzimu. Tiyenera kuyangana pa kuwala konyezimira kwa Choonadi, cimene chinabwera kudzera mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, titathawako kunjira ya chisokonezo cha mu mzimu.
更多

与该标题相关的书籍

The New Life Mission

参加我们的调查

您是如何了解到我们的?