• 所有新生命宣教会 The New Life Mission 网站上的电子书和有声书均可免费下载
  • 探索以多种语言提供的全球性讲道
  • 查看我们已翻译成27种语言的网站
  • 第1卷新修订版已全新推出
Search

免费电子书和有声读物

约翰福音

奇切瓦语  20

Ziphunzitso pa Uthenga wa Yohane (Ⅲ) - Idyani Mnofu Wanga Ndiponso Imwani Magazi Anga

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928239771 | 页码 407

下载免费电子书和有声读物

选择您喜欢的文件格式,安全下载到手机、电脑或平板电脑,随时随地阅读和收听讲道集。所有电子书和有声读物都完全免费。

您可以通过下方播放器收听有声读物。🔻
拥有平装书
在亚马逊购买平装书
Zamkati 

Kalambulabwalo 
1. Kodi Mikate Yaying’noyi ndi Nsomba Ili ndi Nchito Yotani ku Anthu Ambiri (Yohane 6:1-15) 
2. Kukhulupilira mwa Iye Amene Mulungu Anasankha ndi Ntchito ya Mulungu (Yohane 6:16-29) 
3. Gwirani Ntchito ya Chakudya Chokhalitsa Chopereka Moyo Wosatha (John 6:16-40) 
4. Kukhala Mogwirizana ndi Mzimu (Yohane 6:26-40) 
5. Gwirani Ntchito ya Chakudya Chimene Sichikutha Padziko Lapansi (Yohane 6:26-59) 
6. Tiyenera Kudya Mkate Wochoka Kumwamba Mokhulupilira mu Uthenga wa madzi ndi Mzimu (Yohane 6:28-58) 
7. Yesu Khristu, Amene Anakhala Mkate wa Moyo kwa Ife (Yohane 6:41-51) 
8. Kodi Tingadye Bwanji Mnofu wa Yesu? (Yohane 6:41-59) 
9. Khulupilirani Mwa Yesu Amene Anachoka Kumwamba Ngati M’pulumutsi Wanu M’mtima Wanu (Yohane 6:41-51) 
10. Yesu Anatipatsa Moyo Osatha Oona! (Yohane 6:47-51) 
11. Motengelako Mbali M’mgonero Oyera mwa Chikhulupiliro Choyenera (Yohane 6:52-59) 
12. Yesu, Amene Anatipatsa Mkate wa Umoyo (Yohane 6:54-63) 
13. Muyenera Kulalikira Mnofu ndi Magazi a Yesu ku Mamembala Abanja Lanu (Yohane 6:51-56) 
14. Cifukwa N’chiyani Tiyenera Kukhala ndi Moyo? (Yohane 6:63-69) 
15. Tiyenera Kukhala ndi Nzeru Yoyenera ya Choonadi (Yohane 6:60-71) 
 
Yesu Anatipatsa Moyo Osatha Kupitira mu Mnofu Wake ndi Magazi

M’pingo ukusunga masakalamenti awiri olamulidwa ndi Yesu. Oyamba ndi ubatizo, ndipo wina ndi Mgonero Oyera. Tikutengako mbali mu Mgonero kuti tilingalire pa Choonadi cha uthenga chovumvulutsidwa mu mkate wake ndi mu vinyo, mwa kukumbukira uthengau.
Mu chiphikiro cha Mgonero Oyera, tikudya mkate mwa kukhumbukira mnofu wa Yesu, ndipo tikumwa vinyo ngati chiphikiro cha magazi Ake. mwakutero, tanthauzo lenileni la Mgonero Oyera ndi kulimbikitsa chikhulupiliro chathu mu Choonadi chakuti Yesu anatipulumutsa kumachimo adziko ndipo anatipatsa moyo osatha kupitira mu ubatizo Wake ndi imfa Yake pa Mtanda.
Koma, bvuto ndi lakuti pafupi-fupi Akristu onse akutengako mbali mu Mgonero Oyera mwachizolowezi, kopanda ngakhalenso kuzindikira cimene Yesu anatanthauza ndi mawu, “Mnofu Wanga ndi chakudwadi, ndipo magazi Anga ndi chakumwa chenicehni” (Yohane 6:55). Chotero, mkati mwa uthenga wa madzi ndi Mzimu, tikuyenera kulingaliranso pa tanthauzo la Yesu kutilamula kuti tidye mnofu Wake ndi kumwa magazi Ake, ndi kukhulupilira m’menemo.
更多

与该标题相关的书籍

The New Life Mission

参加我们的调查

您是如何了解到我们的?