• 所有新生命宣教会 The New Life Mission 网站上的电子书和有声书均可免费下载
  • 探索以多种语言提供的全球性讲道
  • 查看我们已翻译成27种语言的网站
  • 第1卷新修订版已全新推出
Search

免费电子书和有声读物

马太福音

奇切瓦语  29

ULALIKI PA UTHENGA WABWINO WA MATEYU (III) - NDIWOTANI UTHENGA WABWINO OMWE UMAPANGITSA AKRISTU KUKHALA ANGWIRO?

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928241040 | 页码 386

下载免费电子书和有声读物

选择您喜欢的文件格式,安全下载到手机、电脑或平板电脑,随时随地阅读和收听讲道集。所有电子书和有声读物都完全免费。

您可以通过下方播放器收听有声读物。🔻
拥有平装书
在亚马逊购买平装书
Zamkatimu
 
Mau oyamba 

CHAPITALA 14
1. Milomo Ya Ansembe Auzimu Iyenera Kusunga Chidziwitso Cha Choonadi (Mateyu 14:1-12) 
2. Ndi Chifukwa Chiani Yesu Anachita Chozizwa Cha Mikate Isanu Ndi Nsomba Ziwiri? (Mateyu 14:13-33) 
 
CHAPITALA 15
1. Mulungu Watipatsa Ife Madalitso Opanda Malire (Mateyu 15:32-39) 

CHAPITALA 16
1. Tiyenera Kusamalira Ntchito Ya Mulungu Choyamba (Mateyu 16:21-25) 
2. Chikhulupiliro Chodzikana-Tokha (Mateyu 16:21-27) 
3. Chikondi Cha Petro Kwa Yesu (Mateyu 16:21-27) 
4. Ngati Munthu Afuna Kutsata Ine, Adzikane Yekha! (Mateyu 16:21-28) 
5. Dzikaneni Nokha Ndi Kutsata Ambuye (Mateyu 16:24-27) 
6. Chikhulupiliro Chokha Basi Chimapulumutsa Ife ku Uchimo (Mateyu 16:24-27) 

CHAPITALA 17
1. M’mene Tingalandirire Mzimu Woyera (Mateyu 17:1-13) 
2. Yohane Mbatizi, Amene Anadza M’njira Ya Chilungamo (Mateyu 17:1-13) 

CHAPITALA 18
1. Iwo Amene Chikhulupiliro Chao Chiri Monga Cha Kamwana (Mateyu 18:1-4) 

CHAPITALA 19
1. Iwo Amene Ali Achuma Mu Ntchito Zao Zabwino za Thupi Sangalowe Kumwamba (Mateyu 19:16-30) 

CHAPITALA 20
1. Khalani Chifukwa Cha Uthenga Wabwino wa Madzi Ndi Mzimu (Mateyu 20:20-28) 
 
Mtumwi Mateyu akutiuza ife kuti Mau a Yesu analankhulidwa kwa aliyense m’dziko lino, popeza Iye ankaona Yesu monga Mfumu ya mafumu. Tsopano, Akristu dziko lonse lapansi, amene angobadwa mwatsopano pokhulupilira mu uthenga wabwino wa madzi ndi Mzimu omwe tikufalitsa, indedi akufunitsitsa kudya mkate wamoyo. Koma ndikobvuta kwa iwo kukhala ndi chiyanjano ndi ife mu uthenga wabwino weni weni, popeza iwo onse ali kutali ndi ife. Choncho, kuti tikumane ndi zofunika zauzimu za anthu amenewa a Yesu Kristu, Mfumu ya mafumu,  ulaliki m’buku limeneli wakonzedwa monga mkate watsopano wa moyo kwa iwo kuti usamalire kukula kwao kwauzimu. Mlembi amanena kuti iwo amene alandira chikhululukiro cha machimo ao pokhulupilira m’Mau a Yesu Kristu, Mfumu ya mafumu, ayenera kudya Mau Ake angwiro pofuna kuteteza chikhulupiliro chao komanso kuchita bwino m’miyoyo yao yauzimu. Buku limeneli lidzapereka mkate weni weni wamoyo wauzimu kwa inu nonse amene mwakhala anthu olemekezeka a Mfumu mwa chikhulupiliro. Kudzera mu Mpingo Wake ndi akapolo Ake, Mulungu adzapitiriza kupereka kwa inu mkate umenewu wamoyo. Lolani madalitso a Mulungu akhale pa inu nonse amene mwabadwa mwatsopano mwa madzi ndi Mzimu, amene mukufuna kukhala ndi chiayanjano chauzimu ndi ife mwa Yesu Kristu.
更多
有声书播放器

与该标题相关的书籍

The New Life Mission

参加我们的调查

您是如何了解到我们的?