• 所有新生命宣教会 The New Life Mission 网站上的电子书和有声书均可免费下载
  • 探索以多种语言提供的全球性讲道
  • 查看我们已翻译成27种语言的网站
  • 第1卷新修订版已全新推出
Search

免费电子书和有声读物

马太福音

奇切瓦语  13

ULALIKI PA UTHENGA WABWINO WA MATEYU (II) - KODI TINAKHULUPIRIRA CHIYANI KUTI TILANDIRE CHIKHULULUKIRO CHA MACHIMO?

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928260089 | 页码 512

下载免费电子书和有声读物

选择您喜欢的文件格式,安全下载到手机、电脑或平板电脑,随时随地阅读和收听讲道集。所有电子书和有声读物都完全免费。

您可以通过下方播放器收听有声读物。🔻
拥有平装书
在亚马逊购买平装书
Zamkatimu 
 
Mau Oyamba 

MUTU 9
1. Khulupilirani mwa Yesu Kristu Yemwe Anadza Monga Mulungu Wathu (Mateyu 9:1-13) 
2 .Yesu Yemwe Anadza Kudzapulumutsa Ife, Amanjenje Auzimu (Mateyu 9:1-13) 
3. Chikhulupiliro cha Chipembedzo Motsutsana ndi Chikhulupiliro mu Mphamvu ya Uthenga Wabwino wa Madzi ndi Mzimu (Mateyu 9:1-13) 
4. Antchito a Mulungu (Mateyu 9:35-38) 

MUTU 10
1. Mphamvu Yochiritsa Matenda Onse Imapezeka mu Uthenga Wabwino wa Madzi Ndi Mzimu (Mateyu 10:1-16) 
2. Tiyeni Tikhale Monga Antchito a Mulungu (Mateyu 10:1-8) 

MUTU 11
1. Yohane Mbatizi Sanali Wolephera (Mateyu 11:1-14) 

MUTU 12
1. Yesu Ananena Kuti Iye Amafuna Chifundo Osati Nsembe (Mateyu 12:1-8) 
2. Kodi Mukufuna Kudziwa Kuti Kuchitira Mwano Mzimu Woyera ndi Chiani? (Mateyu 12:9-37) 
3. Tchimo Losakhululukidwa komaso Ntchito ya Obadwa Mwatsopano (Mateyu 12:31-32)
4. Kodi Satana Amafuna Kukhala Kuti? (Mateyu 12:43-50) 

MUTU 13 
1. Fanizo la Mitundu Inayi ya Minda (Mateyu 13:1-9) 
2. Inu Mwaloledwa Kudziwa Zinsinsi za Ufumu wa Kumwamba (Mateyu 13:10-23) 
3. Ufumu wa Kumwamba Ufanizidwa ndi Munthu, Amene Anafesa Mbeu Zabwino M’munda Mwace (Mateyu 13:24-30) 
4. Mphamvu ya Uthenga Wabwino wa Madzi ndi Mzimu (Mateyu 13:31-43) 
5. Ufumu wa Kumwamba Uli Wofanana ndi Cuma Cobisika M’munda (Mateyu 13:44-46)
6. Ufumu wa Kumwamba Uli Wofanana ndi Khoka Loponyedwa m’Nyanja Ndi Kusonkhanitsa Pamodzi Za Mitundu Yonse (Mateyu 13:47-52) 
7. Mariya Ndithudi Si Waumulungu (Mateyu 13:53-58)
 
Mtumwi Mateyu akutiuza ife kuti Mau a Yesu analankhulidwa kwa aliyense m’dziko lino, popeza Iye ankaona Yesu monga Mfumu ya mafumu. Tsopano, Akristu dziko lonse lapansi, amene angobadwa mwatsopano pokhulupilira mu uthenga wabwino wa madzi ndi Mzimu omwe tikufalitsa, indedi akufunitsitsa kudya mkate wamoyo. Koma ndikobvuta kwa iwo kukhala ndi chiyanjano ndi ife mu uthenga wabwino weni weni, popeza iwo onse ali kutali ndi ife. Choncho, kuti tikumane ndi zofunika zauzimu za anthu amenewa a Yesu Kristu, Mfumu ya mafumu, ulaliki m’buku limeneli wakonzedwa monga mkate watsopano wa moyo kwa iwo kuti usamalire kukula kwao kwauzimu. Mlembi amanena kuti iwo amene alandira chikhululukiro cha machimo ao pokhulupilira m’Mau a Yesu Kristu, Mfumu ya mafumu, ayenera kudya Mau Ake angwiro pofuna kuteteza chikhulupiliro chao komanso kuchita bwino m’miyoyo yao yauzimu. Buku limeneli lidzapereka mkate weni weni wamoyo wauzimu kwa inu nonse amene mwakhala anthu olemekezeka a Mfumu mwa chikhulupiliro. Kudzera mu Mpingo Wake ndi akapolo Ake, Mulungu adzapitiriza kupereka kwa inu mkate umenewu wamoyo. Lolani madalitso a Mulungu akhale pa inu nonse amene mwabadwa mwatsopano mwa madzi ndi Mzimu, amene mukufuna kukhala ndi chiayanjano chauzimu ndi ife mwa Yesu Kristu.
更多
有声书播放器

与该标题相关的书籍

The New Life Mission

参加我们的调查

您是如何了解到我们的?