• 所有新生命宣教会 The New Life Mission 网站上的电子书和有声书均可免费下载
  • 探索以多种语言提供的全球性讲道
  • 查看我们已翻译成27种语言的网站
  • 第1卷新修订版已全新推出
Search

免费电子书和有声读物

约翰一书

奇切瓦语  14

Paul C. Jong’s Kukula Mumzimu Mundandanda wa 3 - Kalata Woyamba Wa Yohane (Ⅰ)

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928239269 | 页码 337

下载免费电子书和有声读物

选择您喜欢的文件格式,安全下载到手机、电脑或平板电脑,随时随地阅读和收听讲道集。所有电子书和有声读物都完全免费。

您可以通过下方播放器收听有声读物。🔻
拥有平装书
在亚马逊购买平装书
Zamakati
 
Kalambulabwalo

CHAPITALA 1
1. Yesu Khristu Ndi Mulungu (1 Yohane 1:1-10) 
2. Kodi Mulidi pa Mugwirizano ndi Mulungu? (1 Yohane 1:1-10) 
3. Mitundu Iwiri ya Kumvomereza (1 Yohane 1:8-10) 
4. Kuvomereza mu Choonadi (1 Yohane 1:8-10) 

CHAPITALA 2
1. Yesu Khristu Ndi Mulungu Woona (1 Yohane 2:1-5) 
2. Ambuye Athu Amene Anakhala Mthandizi Wathu (1 Yohane 2:1-17) 
3. Kodi Inu M’kukhala mu Lamulo La Mulungu? (1 John 2:7-11) 
4. Musamakonde Dziko Kapena Zinthu za Mdziko (1 Yohane 2:15-17) 
5. Kodi Adani a Khristu Ndani (1 Yohane 2:18-29) 
 
Mtumwi Yohane ndi mumodzi wa atsogoleri aakulu mumzimu mu Chikhristu. Makalata onse atatu iye analemba akuchitilabe umboni wa wa Choonadi wa cha poyera ndi mumzimu ku woyera mu Mpingo wa Mulungu. Koma muli ndime zina zimene ndi zikosa kuti ife timasulire ndi kumvetsa.
Tingapereke 1Yohane 1:8 ngati chisanzo cha ndime zobvuta mu Makalata ya Yohane: Tikanena kuti: “Tilibe uchimo,” ndiye kuti tikudzinamiza ndipo mwa ife mulibe choonadi.” Ndimeyi ndiyobvuta kumvetsa, maka-maka ngati taigwiritsa nchito ku okhulupilira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu.
Chisanzo chachiwiri ndi 1 Yohane 1:9, “Mulungu ndiwokhulupirika ndiponso wolungama, chotero tikavomereza machimo athu, adzatikhululukira ndi kutiyeretsa ku ntchito zonse zoipa.” Iyi yakhala ndime yakunenedwa pafupipafupi ngati ochimwa akufuna kupereka mfundo zabaibulo za mapemphero awo akulapa. Ndiyeno, ndimeyi ikutanthauza kuti ochimwa afunika kuvomereza machimo awo kuti akhululukidwe kumachimo awo amene anachita kodi? Kapena, kodi chikutanthauza kuti olungama amene okhulupilira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu ayenera kuvomereza machimo awo? Tifunika kukhulupilira ndimeyi malinga ndi kamsulidwe ka Mzimu Woyera, Mlembi wa Baibulo, ndiponso kumalingaliro a Mtumwi Yohane.
Chisanzo cha chitatu cha ndime yobvuta ndi 1 Yohane 2:22, “Kodi wabodza angakhalenso ndani, kuposa amene amatsutsa kuti Yesu ndiye Khristu? Ameneyu ndiye wokana Khristu, amene amakana Atate ndi Mwana.” Ndimeyi ikulankhula za amene ndi adani a Mulungu. Ndimeyi ikufotokoza poyera kuti adani a Mulungu ndi onse aja sakhulupilira kuti Yesu ndi Mulungu. Ndipo ichi chikutanthauzanso kuti sakuthokoza Atate a Yesu Khristu ngati Mulungu.
Chachinayi ndi 1 Yohane 3:6 imene ikuti, “Yense wakukhala mwa Iye sachimwa yense wakuchimwa sanamuone Iye, ndipo sanamdziwe Iye.” Apa, ngati taona mawu, yense wakukhala mwa iye,” ndimeyi akuperekedwa ku olungama amene anayeretsedwa kumachimo awo onse mwa kukhulupilira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu. Olungama sangakane chikhulupiliro chawo muzokhoma zilizonse cifukwa akukhulupilira mu uthenga woona. Kodi kungakhaledi ena amene sakuchita machimo ndi mathupi awo? Aliyense akuchita uchimo. Koma, okhulupilira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu sangachite uchimo otero ngati wakukana uthenga woona.
更多

与该标题相关的书籍

The New Life Mission

参加我们的调查

您是如何了解到我们的?