Search

VITABU PEPE NA VITABU VYA SAUTI BURE

Ufunuo

Chichewa  8

Ndemanga ndi Ulaliki pa Buku la Chibvumbulutso - KODI NYENGO YA WOTSUTSAKRISTU, KUFERA CHIKHULUPILIRO, MKWATULO KOMANSO UFUMU WA ZAKACHIKWI IKUDZA? (II)

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928231522 | Kurasa 499

Pakua vitabu pepe na vitabu vya sauti BURE

Chagua muundo wa faili unaopendelea na upakue salama kwenye simu yako, kompyuta au kompyuta kibao kusoma na kusikiliza mkusanyiko wa mahubiri wakati wowote na mahali popote. Vitabu vyote pepe na vitabu vya sauti ni bure kabisa.

Unaweza kusikiliza kitabu cha sauti kupitia kichezaji hapa chini. 🔻
Miliki kitabu kilichochapishwa
Nunua kitabu kilichochapishwa kwenye Amazon
Zamkatimu 

Mau Oyamba 

MUTU 8
1. Malipenga Omwe Amalengeza za Milili Isanu ndi Iwiri (Chibvumbulutso 8:1-13) 
2. Kodi Milili ya Malipenga Asanu ndi Awiri ndi Yeniyeni? 

MUTU 9
1. Mlili Wochokera Kudzenje la Phompho (Chibvumbulutso 9:1-21) 
2. Khalani Ndi Chikhulupiliro Cholimba Mtima Kumapeto kwa Nthawi 

MUTU 10
1. Kodi Mukudziwa Kuti Nthawi ya Mkwatulo Ndi Yotani? (Chibvumbulutso 10:1-11) 
2. Kodi Mukudziwa Pamene Mkwatulo wa Oyera Mtima Udzachitika? 

MUTU 11
1. Kodi Mitengo Iwiri ya Azitona ndi Aneneri Awiri Ndindani? (Chibvumbulutso 11:1-19) 
2. Chipulumutso cha Anthu a ku Israyeli 

MUTU 12
1. Mpingo wa Mulungu Omwe Udzavulazidwa Kwambiri M’tsogolo (Chibvumbulutso 12:1-17) 
2. Landirani Kuphedwa Kwanu ndi Chikhulupiliro Cholimba 

MUTU 13
1. Kuonekera kwa Wotsutsakristu (Chibvumbulutso 13:1-18) 
2. Maonekedwe a Wotsutsakristu 

MUTU 14
1. Matamando a Ofera Chikhulupiliro Oukitsidwa ndi Okwatulidwa (Chibvumbulutso 14:1-20) 
2. Kodi Oyera Mtima Ayenera Kuchita Chiani ku Maonekedwe a Wotsutsakristu? 

MUTU 15
1. Oyera Mtima Omwe Amayamika Ntchito Zodabwitsa za Ambuye mu Mlengalenga (Chibvumbulutso 15:1-8) 
2. Gawo Logawanitsa Tsogolo Lamuyaya 

MUTU 16
1. Chiyambi cha Milili ya Mbale Zisanu ndi Ziwiri (Chibvumbulutso 16:1-21) 
2. Chomwe Muyenera Kuchita Mbale Zisanu ndi Ziwiri Zisanathiridwe Ndi… 

MUTU 17
1. Chiweruzo cha Mkazi Wachigololo Wokhala pa Madzi Ambiri (Chibvumbulutso 17:1-18) 
2. Tipereke Chidwi Chathu pa Chifuniro Chake 

MUTU 18
1. Dziko la Babulo Lagwa (Chibvumbulutso 18:1-24) 
2. “Turukani M’menemo, Anthu Anga, Kuti Mungalandireko ya Milili Yake” 

MUTU 19
1. Ufumu Umene Udzalamuliridwa ndi Wamphamvuyonse (Chibvumbulutso 19:1-21) 
2. Olungama Okha Angathe Kudikilira mwa Chiyembekezo kwa Kristu Kuti Abwerenso 

MUTU 20
1. Chinjoka Chidzatsekeredwa ku Dzenje la Phompho (Chibvumbulutso 20:1-15) 
2. Kodi Tingadutse Bwanji Kuchoka ku Imfa Kufika ku Moyo? 

MUTU 21
1. Mzinda Woyera Wotsika Kuchokera Kumwamba (Chibvumbulutso 21:1-27) 
2. Tiyenera Kukhala ndi Chikhulupiliro Chomwe Chimatsimikizidwa ndi Mulungu 

MUTU 22
1. Kumwamba ndi Pansi Patsopano, Kumene Madzi a Moyo Amayenda (Chibvumbulutso 22:1-21) 
2. Khalani Okondwa ndi Olimba mu Chiyembekezo cha Ulemerero 

Mau Oonjezera
1. Mafunso ndi Mayankho 
 
Akristu Ambiri matsiku ano okhulupilira mchiphunzitso cha kukwatulidwa kosaona-chisautso. Cifukwa iwo okhulupilira mchiphunzitsocho chachinyengo chowaphunzitsa kuti iwo adzatengedwa Chisautso Chachikulu cha zaka 7 chisanabwere, okhala moyo wachipembezo osatangwanidwa okhutilisidwa.
Koma kukwatulidwa kwa oyera kudzachitika pokhapo miliri ya malipenga 7 yatsiliza nchito yake mpaka muliri wa 6 wonse utathilidwa-ndi pamene, kukwatulidwa kudzachitika Wosusa Khristu ataonekera pakati mtsokonozo wa dziko lonse lapansi ndipo oyera obadwa-mwatsopano ataphedwa, ndiponso ngati lipenga la 7 lalizidwa. Ndi pa nthawi imeneyo pamene Yesu adzatsika kuchoka Kumwamba, ndipo chiukitso ndi kukwatulidwa kwa oyera obadwa-mwatsopano chidzachitika (1 Atesalonika 4:16-17).
Pa tsikuli, wina aliyense mdzikoli lapansi adzakhala ali kuimilira pa mphatukano za miseu wa kumalo ake osatha. Olungama amene anabadwa mwatsopano pokhulupilira mu “uthenga wa madzi ndi Mzimu” adzaukitsidwa ndi kukwatulidwa, ndipo adzakhala olowa mu Ufumu wa zaka Chikwi chimodzi ndiponso mu Ufumu osatha wa Kumwamba, koma ochimwa amene sanakwanitse kutengako mbali mchiukitsochi choyamba adzakumana ndi chilango chachikulu cha mbale 7 chothilidwa ndi Mulungu ndi kuponyedwa mmoto osatha wa mgehena
Choncho, tsopano muyenera kuchokamo mu ziphunzitso zonse za chinyengo za zipembezo ndiponso mchilakolako ndi mu zinthu zosokonezeka za dzikoli, ndi kulowa mu Mawu oona a Mulungu. Ndikhulupilira ndi kupemphera kuti powerenga mndandanda wa ma uthenga anga a madzi ndi Mzimu, monse mdzaikidwa dalitso la machimo anu onse kuchotsedwa, ndi lolandira kubwera kwachiwiri kwa Ambuye athu kopanda mantha.
Zaidi
Mchezaji wa vitabu vya sauti

Vitabu vinavyohusiana na kichwa hiki

The New Life Mission

Shiriki katika utafiti wetu

Ulitujuaje?