• 所有新生命宣教會 The New Life Mission 網站上的電子書和有聲書均可免費下載
  • 探索以多種語言提供的全球性講道
  • 查看我們已翻譯成27種語言的網站
  • 第1、2卷新修訂版已全新推出
Search

免費電子書和有聲讀物

馬太福音

奇切瓦語  12

ULALIKI PA UTHENGA WABWINO WA MATEYU (I) - KODI NDIPATI PAMENE M’KRISTU ANGATHE KUKHALA NDI KUKAMBIRANA KWA PAMTIMA NDI AMBUYE?

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928238859 | 頁碼 406

下載免費電子書和有聲讀物

選擇您喜歡的文件格式,安全下載到手機、電腦或平板電腦,隨時隨地閱讀和收聽講道集。所有電子書和有聲讀物都完全免費。

您可以通過下方播放器收聽有聲讀物。🔻
擁有平裝書
在亞馬遜購買平裝書
Zamkatimu 

Mau Oyamba 

MUTU 1
1. Mbadwo wa Yesu Kristu (Mateyu 1:1-6) 
2. Tiyeni Tiyamike Ambuye Wanthu Amene Anabwera Kudzatipulumutsa Ife (Mateyu 1:18-25) 
3. Yesu Amene Anabadwa Mwa Mzimu Woyera (Mateyu 1:18-25) 

MUTU 2
1. Kodi Tingakumane Kuti ndi Ambuye Moyenera? (Mateyu 2:1-12)

MUTU 3
1. Kufalitsa Uthenga Wabwino Oona Ndi Ntchito Yolungama Ya Yesu (Mateyu 3:1-17) 
2. Yesu Amene Anabwera Kuti Afafanize Machimo Anu (Mateyu 3:13-17) 

MUTU 4
1. Dalitso Ndi Kuopa Mulungu ndi Kutumikira Mulungu (Mateyu 4:1-11) 

MUTU 5 
1. Ulaliki pa Phiri (Mateyu 5:1-16)

MUTU 6
1. Chiphunzitso cha Ambuye pa Pemphero (1) (Mateyu 6:1-15) 
2. Chiphunzitso cha Ambuye pa Pemphero (2) (Mateyu 6:5-15) 
3. Khalani ndi Mitima Yanu pa Ambuye (Mateyu 6:21-23)
4. Musadere Nkhawa za Moyo Wanu, Koma Dalirani mwa Mulungu Yekha (Mateyu 6:25-34) 
5. Zikwanire Tsiku Zobvuta Zake (Mateyu 6:34) 

MUTU 7
1. Pokhulupilira mu Mphamvu ya Uthenga Wabwino, Tiyenera Kulowa Kudzera mu Cipata Copapatiza (Mateyu 7:13-14) 
2. Kodi Tidzachita Chiani Ngati Tidzakanidwa ndi Ambuye pa Tsiku Lotsiriza? (Mateyu 7:21-23) 
3. Chikhulupiliro Chomwe Chingathe Kuchita Chifuniro cha Mulungu Atate (Mateyu 7:20-27) 
4. Tingathe Kulowa Kumwamba Pokhapo Ngati Tadziwa Chifuniro cha Atate ndi Kukhulupilira mu Icho (Mateyu 7:21-27) 
5. Chenjerani ndi Aneneri Onyega Omwe Amangofuna Ndalama Zanu (Mateyu 7:13-27) 

MUTU 8
1. Machiritso a Akhate Auzimu (Mateyu 8:1-4) 
2. “Mungonena Mau” (Mateyu 8:5-10) 
3. Tsatani Ambuye Poyamba (Mateyu 8:18-22) 

Mtumwi Mateyu akutiuza ife kuti Mau a Yesu analankhulidwa kwa aliyense m’dziko lino, popeza Iye ankaona Yesu monga Mfumu ya mafumu. Tsopano, Akristu dziko lonse lapansi, amene angobadwa mwatsopano pokhulupilira mu uthenga wabwino wa madzi ndi Mzimu omwe tikufalitsa, indedi akufunitsitsa kudya mkate wamoyo. Koma ndikobvuta kwa iwo kukhala ndi chiyanjano ndi ife mu uthenga wabwino weni weni, popeza iwo onse ali kutali ndi ife. Choncho, kuti tikumane ndi zofunika zauzimu za anthu amenewa a Yesu Kristu, Mfumu ya mafumu, ulaliki m’buku limeneli wakonzedwa monga mkate watsopano wa moyo kwa iwo kuti usamalire kukula kwao kwauzimu. Mlembi amanena kuti iwo amene alandira chikhululukiro cha machimo ao pokhulupilira m’Mau a Yesu Kristu, Mfumu ya mafumu, ayenera kudya Mau Ake angwiro pofuna kuteteza chikhulupiliro chao komanso kuchita bwino m’miyoyo yao yauzimu. Buku limeneli lidzapereka mkate weni weni wamoyo wauzimu kwa inu nonse amene mwakhala anthu olemekezeka a Mfumu mwa chikhulupiliro. Kudzera mu Mpingo Wake ndi akapolo Ake, Mulungu adzapitiriza kupereka kwa inu mkate umenewu wamoyo. Lolani madalitso a Mulungu akhale pa inu nonse amene mwabadwa mwatsopano mwa madzi ndi Mzimu, amene mukufuna kukhala ndi chiayanjano chauzimu ndi ife mwa Yesu Kristu.
更多
有聲書播放器

與該標題相關的書籍

The New Life Mission

參加我們的調查

您是如何得知我們的?