Zamkati
Kalambulabwalo
CHAPITALA 1
1. Yesu Khristu, Moyo Wathu (Yohane 1:1-4)
2. Tiyenera Kukhala Obadwa a Mulungu (Yohane 1:12-18)
3. Chikondi cha Mulungu Chovumbulutsidwa Kudzera mwa Yesu, Mwana Wobadwa Yekha (Yohane 1:15-18)
4. Choonadi Chimene Yohane M’batizi Anachitira Umboni (Yohane 1:19-28)
5. Umboni wa mu Baibulo Wakuti Yesu Ananyamura Machimo Onse Adziko (John 1:29-39)
6. Chikhulupiliro Chokhulupilira mu Mawu a Mulungu Okha (Yohane 1:1-8)
7. Sitingakhale Okondwera Koposa Kumeneku (Yohane 1:29-31)
8. Kodi ndi Mtundu wa Mumaonekedwe Otani Amene Mulengi Wathu Amatiyendera Nawo? (Yohane 1:1-13)
9. Kodi Yohane M’batizi N’ndani? (Yohane 1:19-42)
CHAPITALA 2
1. Tikukondwera Ngati Tavomera Yesu M’mitima Yathu (Yohane 2:1-11)
2. Tingalawe Madalitso Ochokera kwa Mulungu Pokhapo Ngati Tikumverera Mawu a Mulungu (Yohane 2:5)
CHAPITALA 3
1. Tiyenera Kubadwa Mwatsopano mwa Kudziwa ndi Kukhulupilira Mnjirayi (Yohane 3:1-6)
2. Kodi Mumakhulupirira mu Uthenga wa Madzi ndi Mzimu Wopatsidwa Ndi Mulungu? (Yohane 3:1-8)
3. Kodi Ndichiyani Chimapangitsa Kukhala Chotheka kuti Tibadwe Mwatsopano? (Yohane 3:1-15)
4. Kodi M’kuchidziwadi Chikondi cha Mulungu? (Yohane 3:16)
5. Tiyeni Tigwire Nchito ya Uzimu mwa Chikhulupiliro (Yohane 3:16-17)
Chikodi Chovumbulutsidwa Kupitira mwa Yesu Khristu
Chinalembedwa, “Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse, Mulungu wobadwa yekha amene ali pachifuwa cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu” (Yohane 1:18).
Yesu anaulura mokwana bwanji chikondi cha Mulungu kwaife! Kodi ndi choona cheni-cheni chotani chachipulumutso chili mu uthenga wa madzi ndi Mzimu! Sitinadzitsutse polandira chipulumutso kupitira mu chikhulupiliro chathu mwa Yesu, amene anabwera mwa madzi ndi magazi. (1 Yohane 5:6).
Ndikhulupilira kuti nonsenu m’kukhulupilira mwa Yesu Khristu amene anavumbulutsa chikondi cha Mulungu, sungani chikhulupiliro mu chikondi Chake m’mitima yanu, ndipo nthawi zonse mkhale ndi moyo pacifukwa cha kufalitsa chikondicho. Ndikhulupilira kuti mdzafuna dalitso la chikhulukiro cha uchimo mwa kukumana ndi Mulungu kupitira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu.
More