Zamkati
Kalambulabwalo
CHAPITALA 3
1. Mulungu Wathu Amene Anabwera kwa Ife ndi Chikondi Chodabwitsa (1 Yohane 3:1-8)
2. Kodi N’chimo la Mtundu Wotani Limene Sitiyenera Kuchita Pamaso pa Mulungu? (1 Yohane 3:9-16)
3. Iye Amene Asunga Malamulo a Mulungu Akhala mwa Iye (1 Yohane 3:17-24)
CHAPITALA 4
1. Yesani Mizimu Ngati Ichokera Mwa Mulungu (1 Yohane 4:1-6)
2. Tiyenera Kukhala Motani Kuchokera Tsopanoli? (1 Yohane 4:7-13)
3. Tiyenera Kukhala mu Chikondi Cha Mulungu (1 Yohane 4:16-21)
CHAPITALA 5
1. Kodi N’choonadi Chotani Chimene Chikutimasura Kumachimo Athu Onse? (1 Yohane 5:1-4)
2. Kodi N’ndani Wobadwa Mwa Mulungu? (1 Yohane 5:4-8)
3. Kodi Tikukhulupilira mu Chiyani? (1 Yohane 5:1-11)
4. Kodi Choonadi Cimene Chinatiombola Kumachimo Athu Onse Ndichotani? (1 Yohane 5:1-12)
5. Umboni Woona Umene Ukutipulumutsa Kumachimo Athu Onse (1 Yohane 5:8-13)
6. Ngati M’bale Akuchita Tchimo Losabweretsa Imfa, Timupempherere kwa Mulungu Kuti Azimupatsa Iye Moyo (1 Yohane 5:16-19)
7. Iye Ndi Mulungu Woona Ndiponso Moyo Wosatha (1 Yohane 5:20)
8. Ngakhale Nthawi Zonse Tingakhale Osowekera, Chikondi Changwiro Cha Mulungu Chinatiombola Kumachimo Adziko (1 Yohane 5:1-21)
Ngati ndiwe Mkristu woona, ufunika kudziwa chikondi cha kwambiri koposa mwa ziphunzitso chabe. Onse amene odziwa ndi kukhulupilira Yesu ngati M’pulumutsi wawo ayenera kudziwa chikondi cha Mulungu mwathunthu mu chikhululukiro chawo cha machimo cimene chinakwanilitsidwa kupitira mu Mawu a uthenga wa madzi ndi Mzimu. Tiyenera kukhala okhulupilira oona mu uthengawu oona kotero kuti tidziwe chikondi cha Mulungu mozama. Mu uthengau oona, chikondi cha Mulungu chikuvumbulutsidwa mwathunthu ndiponso mozama. Ngati tikufuna kudziwa Mulungu ngati chikondi, kuzindikira kwathu kuyenera kuchokera ku chikondi chathunthu cha Mulungu kwa ife cimene chinavumbulutsidwa mu Choonadi cha uthenga wa madzi ndi Mzimu. Ndipokhapo pamene tingatengere anthu ena ku chikondi choona cha Mulungu.
Monga mmene chinalembedwa mu Mawu a Mulungu, madzi akutanthauza ubatizo wa Yesu umene Iye analandira kwa Yohane M’batizi, ndipo mwazi akutanthauza chiweruzo cimene Iye analandira cifukwa cha machimo athu onse. Ndiponso, umboni wa chipulumutso chathu ukugona mu Mzimu Woyera, madzi, ndi mwazi (1 Yohane 5:8). Mautumiki a madzi, mwazi, ndi Mzimu Woyera ndi aja a Mulungu kupitira mu ameneo Iye anaombora ochimwa kumachimo awo onse.
ပိုများသော