Zamkati
Kalambulabwalo
CHAPITALA 4
1. Ndife Amene Sadzalawa Imfa, Kusangalala Ndi Moyo Wosatha (Agalatiya 4:1-11)
2. Kodi Inu ndi Ine Tili ndi Mtundu wa Chikhulupirilo Chofanana ndi Chimene Abulahamu Anali Nacho? (Agalatiya 4:12-31)
3. Musabwererenso Kumfundo Zofoka ndiponso Zopanda Pake Zadziko (Agalatiya 4:1-11)
4. Ndife Olowa Cholowa cha Mulungu (Agalatiya 4:1-11)
CHAPITALA 5
1. Khalani mwa Khristu Kukhulupirira mu Uthenga wa Madzi ndi Mzimu (Agalatiya 5:1-16)
2. Phindu la Chikhulupiliro Chogwira Nchito Kudzera M’chikondi (Agalatiya 5:1-6)
3. Khalani mwa Zikhumbo za Mzimu (Agalatiya 5:7-26)
4. Zikhumbo za Mzimu Woyera ndi Zija za Thupi (Agalatiya 5:13-26)
5. Yendani mwa Chikhumbo cha Mzimu (Agalatiya 5:16-26)
6. Chipatso cha Mzimu Woyera (Agalatiya 5:15-26)
7. Musakhale mwa Ulemerero Opanda Pake Koma Funani Ulemerero wa Ufumu wa Mulungu (Agalatiya 5:16-26)
CHAPITILA 6
1. Gawanani mu Nchito Zonse Zabwino za Mulungu (Galatiya 6:1-10)
2. Ife Tokha Tiyenera Kutaya Kutali Chikhulupiriro cha Mapemphero Akulapa Pozindikira kuti ndi Kulakwa (Galatians 6:1-10)
3. Tiyeni Titumikire Mulungu Monyamulirana Zolematsa za Wina ndi Mzake (Agalatiya 6:1-10)
4. Ambuye Anatipulumutsa Osati Kudzera mu Mwazi Wake wa pa Mtanda Okha, Koma Kudzera mu Uthenga wa Madzi ndi Mzimu (Agalatiya 6:11-18)
5. Tiyeni Tilalikire Uthenga wa Madzi ndi Mzimu mwa Kumvetsetsa Koyenera (Agalatiya 6:17-18)
Chiphunzitso cha Kulapa Ndichokwanira Kukupanhitsani kuti Mtore Matenda a Kuuzimu.
Anthu mdziko lonse ali ndi mantha ndi tudoyo ngati SARS, cifukwa angafe mwamusanga mwa kuonetsedwa ku tudoyo totero tosaoneka.
Chimodzimodzi, Akristu masiku ano kudzungulira dziko lonse akufa mu mathupi awo ndiponso mu mzimu mwa kudwara ndi chiphunzitso cha kulapa. Kodi munali kudziwa kuti chiphunzitso cha kulapa ndi cholakwika moteromu?
Kodi mkudziwa amene anapangitsa Akristu kugwera mu dzenje lolowelera la chisokonezo cha mu mzimu. Ndi Akristu ochimwa iwo okha amene akupemphera mapemphero akulapa tsiku ndi tsiku kuti ayeretsedwe kumachimo awo a payekha payekha pamene akunena kuti okhulupilira mwa Yesu Khristu ngati M’pulumutsi wawo.
Chotero, muyenera kulandira chikhululukiro cha machimo mwa kukhulupilira mu Mawu a uthenga wa madzi ndi Mzimu umene Mulungu anatipatsa pachiyambi. Si muyenera kutaya mpata odalitsidwa okhala obadwa mwatsopano. Tonsefe tiyenera kumasulidwa kuchisokonezo cha mu mzimu mwa kukhulupilira mu Choonadi cha uthenga wa madzi ndi Mzimu. Tiyenera kuyangana pa kuwala konyezimira kwa Choonadi, cimene chinabwera kudzera mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, titathawako kunjira ya chisokonezo cha mu mzimu.
ပိုများသော