Zamkati
Kalambulabwalo
CHAPTER 1
1. Baibulo Ndilo Mawu a Chipulumutso, Osati Buku la Maphunziro a Zachilengedwe (Genesis 1:1-2)
2. Kodi Munakhala Kuwala Mu Uthenga wa Choonadi? (Genesis 1:2-3)
3. Kuchoka Ku Mphamvu ya Mdima kulowa Mu Ufumu wa Mwana (Genesis 1:2-5)
4. Tsiku Loyamba: Pachiyambi Mulungu Analenga Kumwamba ndi Dziko Lapansi (Genesis 1:1-5)
5. Madzi A Pamwamba pa Thambo ndi Madzi a Pansi pa Thambo (Genesis 1:6-8)
6. Mulungu Analekanitsa Madzi Pa Tsiku Lachiwiri (Genesis 1:6-8)
7. Kukwanilitsa Chifuniro cha Mulungu (Genesis 1:9-13)
8. Kuti Tilowe M’kati Mwa Ntchito ya Mulungu (Genesis 1:9-13)
9. Tingapulumutsidwe ku Uchimo Wathu Onse Pokhapo Ngati Tikudziwa Kuipa Kwathu Konse (Genesis 1:9-13)
10. Kodi N’chiyani Chimene Atumiki a Mulungu Amene Akhulupilira mu Uthenga wa madzi ndi Mzimu Ayenera Kuchita (Genesis 1:14-19)
11. Mulungu Akutipanga Kukhala Ziwiya Zaulemu (Genesis 1:16-19)
12. Olungama Adzakhala Ndi Moyo Mwachikhulupiliro Chokha (Genesis 1:20-23)
13. Ikani Mitima Yanu Pamaso pa Mulungu (Genesis 1:20-23)
14. Miyoyo ya Anthu a Chikhulupiliro Amene Akhulupilira mu Mawu a Mulungu Ndi Mitima Yawo (Genesis 1:20-23)
15. Chifukwa Chimene Mulungu Anatipangira Mofanana ndi Chifanizo Chake (Genesis 1:24-31)
16. Tinapangidwa M’chifanizo cha Mulungu (Genesis 1:24-31)
Mu Buku la Genesis, cholinga cimene Mulungu anatilengera chikupezeka. Ngati omanga manyumba apanga maonekedwe a nyumba kapena olemba ailemba, poyamba akukhala ndi nchito imene adzakwanilitsidwa mu maganizo awo sanayambedi kugwira nchito pa nchito yawoyo. Momwemo, Mulungu wathu nayenso anali nacho chipulumutso chathu mu maganizo Ache cha anthu ngakhalenso asanalenge kumwamba ndi dziko lapansi, ndipo Iye anapanga Adamu ndi Eve mwa cholingachi mu maganizo. Mulungu anali kufuna kumasulira kwa ife a malo a Kumwamba, amene sakuoneka ndi maso athu a thupi, mwakupanga chifanizo cha malo a padziko lapansi cimene tonse tingachione ndi kuchimvetsetsa.
Ngakhalenso dziko lisanakhalepo, Mulungu anali kufuna kupulumutsa anthu mwa ngwiro mwa kuwapatsa uthenga wa madzi ndi Mzimu ku mtima wa munthu aliyense. Chotero ngakhale kuti anthu onse anapangidwa kuchoka kufumbi, ayenera kuphunzira ndi kudziwa Choonadi cha uthenga wa madzi ndi Mzimu kuti aphindulire miyoyo yawo. Ngati anthu akupitiliza kukhala kopanda kudziwa ulamuliro wa Kumwamba, adzataya osati zinthu zokha zadziko lapansi, komanso zinthu zonse zimene zili Kumwamba.
ပိုများသော