Zamkati
Kalambulabwalo
CHAPITALA 2
1. Madalitso Amene Mulungu Anatipatsa (Genesis 2:1-3)
2. Maganizo a Munthu Ali Ngati Nkhungu (Genesis 2:4-6)
3. Tinakumana ndi Yesu Khristu Mkwati Wathu (Genesis 2:21-25)
CHAPITALA 3
1. Choonadi Sichisintha Ngakhale Anthu Ambiri Angachikane Motani (Genesis 3:1-4)
2. Uchimo Unadzalowa Mdzikoli (Genesis 3:1-6)
3. Kodi Chikhulupiliro Chathu Tiyenera Kuimilika Poti? (Genesis 3:1-7)
4. Mphamvu ya Chikhulupiliro mwa Mulungu (Genesis 3:1-7)
5. Tingagonjetse Satana mwa Chikhulupiliro Choona Chokha (Genesis 3:1-7)
6. Tiyenera Kugonjetsa Chinyengo cha Satana Mwa Kukhulupilira mu Uthenga Oona (Genesis 3:1-7)
7. Masiku Onse Funani Chophindulira Mulungu Chokha (Genesis 3:1-24)
8. Machimo Athu Anatsukidwa Mwakukhulupilira mu Uthenga Weniweni (Genesis 3:8-10)
9. Tiyenera Kukhala ndi Moyo Malinga ndi Zokhumba za Mzimu Woyera (Genesis 3:8-17)
10. Kodi Chabwino Chenicheni Ndi Choipa Chenicheni N’chiyani? (Genesis 3:10-24)
11. Chisamaliro cha Mulungu (Genesis 3:13-24)
12. Kodi Tiyenera Kukhala ndi Moyo Mwa Ndani? (Genesis 3:17-21)
Mu Buku la Genesisi, cholinga cha cimene Mulungu anatilengera chipezeza. Pamene architekicha alemba nyumba kapena wolemba adinda chithunzi, poyamba amayamba akhala ndi nchito ija imene angakwanilitsidwe mu maganizo yawo sanayambe kugwira nchito pa polonjekiti yawo. Monga chotero, Mulungu nayenso anali ndi chipulumutso chathu mu maganizo Ake ngakhale Iye asanalenge kumwamba ndi dziko lapansi, ndipo anapanga Adamu ndi Hava mu cholinga Chake cha mu maganizo. Ndipo Mulungu anafotokoza za malo a Kumwamba, amene samaoneka ndi maso athu a thupi, polemba mndandanda wa malo apadziko lapansi amene tingayaone tonse ndi kumvesetsa.
Ngakhale kuchokera pamaziko ya dziko, Mulungu anali kufuna kupulumutsa anthu molungama popereka uthenga wa madzi ndi Mzimu ku mtima wa aliyense. Kotero ngakhale anthu onse anapangidwa kuchokera kufumbi, ayenera kuphunzira ndi kudziwa Choonadi cha uthenga wa madzi ndi Mzimu kuti miyoyo yawo yisangalale. Anthu akapitiriza kukhala opanda kudzindikira mphamvu za Kumwamba, adzataya zinthu osati za padziko lapansi zokha, komaso ndi zonse za Kumwamba.
ပိုများသော