• 所有新生命宣教會 The New Life Mission 網站上的電子書和有聲書均可免費下載
  • 探索以多種語言提供的全球性講道
  • 查看我們已翻譯成27種語言的網站
  • 第1、2卷新修訂版已全新推出
Search

免費電子書和有聲讀物

約翰福音

奇切瓦語  19

Ziphunzitso pa Uthenga wa Yohane (Ⅱ) - Chikondi cha Mulungu Chovumbulutsidwa Kupitira mwa Yesu, Mwana Wobadwa Yekha (Ⅱ)

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928239757 | 頁碼 0

下載免費電子書和有聲讀物

選擇您喜歡的文件格式,安全下載到手機、電腦或平板電腦,隨時隨地閱讀和收聽講道集。所有電子書和有聲讀物都完全免費。

您可以通過下方播放器收聽有聲讀物。🔻
擁有平裝書
在亞馬遜購買平裝書
Zamkatimu

Kulambulabwalo 

CHAPITALA 3
1. Tiyenera Kubadwa Mwatsopano Mwa Kukhulupilira mu Uthenga wa Madzi ndi Mzimu (Yohane 3:1-15) 
2. Ambuye Athu Anabwera Padzikoli Kudzatipulumutsa Kumachimo Adziko (Yohane 3:14-21) 
3. Kodi Tiyenara Kukhulupilira M’chiyani Pamaso pa Mulungu? (Yohane 3:21) 
4. Mulungu Wathu Ndiye Ambuye Amene Anatipatsa Umoyo Wosatha, Woona (Yohane 3:35-36) 

CHAPITALA 4
1. Ambuye Amene Amathetsa Mabvuto Athu onse (Yohane 4:3-19) 
2. Kodi Ndi M’chiyani M’mene Mitima Yathu Ikupeza Chikhutilitso? (Yohane 4:10-24) 
3. Madzi Amoyo Amene Amapangitsa Munthu Kuti Asamvenso Ludzu (Yohane 4:13-26, John 4:39-42) 
4. Kodi N’mtundu Otani wa Chikhulupiliro Umene Tifunika wa Chitsitsimutso Chathu cha Uzimu? (Yohane 4:19-26)
5. Mawu a Yesu Ndi Mawu a Mulungu (Yohane 4:46-54) 

CHAPITALA 5
1. Sitiyenera Kubwereranso Ku Chiyuda (Yohane 5:10-29) 
2. Ambuye Ayendera Dziwe la ku Betiseda (Yohane 5:1-9) 

CHAPITALA 6
1. Gwirani Nchito ya Kuti Mpeze Chakudya Chokhalitsa Chopeleka Moyo Wosatha (Yohane 6:16-40) 
 
Chikodi Chovumbulutsidwa Kupitira mwa Yesu Khristu

Chinalembedwa, “Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse, Mulungu wobadwa yekha amene ali pachifuwa cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu” (Yohane 1:18).
Yesu anaulura mokwana bwanji chikondi cha Mulungu kwaife! Kodi ndi choona cheni-cheni chotani chachipulumutso chili mu uthenga wa madzi ndi Mzimu! Sitinadzitsutse polandira chipulumutso kupitira mu chikhulupiliro chathu mwa Yesu, amene anabwera mwa madzi ndi magazi. (1 Yohane 5:6).
Ndikhulupilira kuti nonsenu m’kukhulupilira mwa Yesu Khristu amene anavumbulutsa chikondi cha Mulungu, sungani chikhulupiliro mu chikondi Chake m’mitima yanu, ndipo nthawi zonse mkhale ndi moyo pacifukwa cha kufalitsa chikondicho. Ndikhulupilira kuti mdzafuna dalitso la chikhulukiro cha uchimo mwa kukumana ndi Mulungu kupitira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu.
更多

與該標題相關的書籍

The New Life Mission

參加我們的調查

您是如何得知我們的?